Umatha Daily

Umatha Daily African Fastest Growing Entertainment Brand
(16)

11/07/2024

Koma chifukwa chani amafuna angowona laku manja lokha osati onse?🤔.
Tulo silikubwela

11/07/2024

Komatu zomwe wapanga MAFA uku nde sizoona
Mphekesera ikuti Anuwake a Lodge mpaka akasiya nkhani ku Police , akuti akufuna ma Key 🗝️ awo

11/07/2024

Basi Tiyeni tilire kenako tigone asisi. Mawa ofunika kuyesa kuphoda kwambiri komaso ka Perfume kabwino, Mamuna apezeka

Lotani kuti anthu awa ndindani? Talotani tikufuna tiwagulire mathalauza ena 🙄
11/07/2024

Lotani kuti anthu awa ndindani? Talotani tikufuna tiwagulire mathalauza ena 🙄

Gwamba and his wife zawo phee 🙄Photo Credit : Charisma
11/07/2024

Gwamba and his wife zawo phee 🙄

Photo Credit : Charisma

Mwayikumbukila CITY BUS?? ija ankati izikhala ndi mtengo umodzi koma ukwela tsiku lonse.Pano ikuyenda Mitundu mitundu. t...
11/07/2024

Mwayikumbukila CITY BUS?? ija ankati izikhala ndi mtengo umodzi koma ukwela tsiku lonse.

Pano ikuyenda Mitundu mitundu. town inayilaka

Time is moving so fast 🙄

11/07/2024

Mwayamba kunamizila FDH kuti sikugwilatu. Koma chilungamo ndichoti mulibe ndalama zoti mubwenzere ngongole. Koma Graduate ngongole zikupha🙌

Asaaa koma mbwiyache akuoneka  nkhope yong'aluratu.. 😃
11/07/2024

Asaaa koma mbwiyache akuoneka nkhope yong'aluratu.. 😃

11/07/2024

Mwati ku TikTok ko zikukhala bwanji ?

11/07/2024

Woyimba wina Banja lake lasokonekela dzulo, akuti Cheating too much.
Koma we have decided to mind our own business on this issue

11/07/2024

We still don't understand why some of you buy expensive toilet papers🤦🏾🧻🚽
MORNING🙄!

Mwina ifeyo pakamwa too much. Koma akulu awawa ku office iyiyi mukuganiza kuti amakataniko?Ali ku page iyi👇https://www.f...
10/07/2024

Mwina ifeyo pakamwa too much. Koma akulu awawa ku office iyiyi mukuganiza kuti amakataniko?

Ali ku page iyi👇https://www.facebook.com/memory.makamo

Takatifunsileni bola musaope nkhope yawo pa profile 🫢

Life Changing foundation ikubwereserani "Cocktail Fundraiser For Charity" ku Blantyre (Golden Peacock) komwe kutakhale l...
10/07/2024

Life Changing foundation ikubwereserani "Cocktail Fundraiser For Charity" ku Blantyre (Golden Peacock) komwe kutakhale live performance band komanso free hd pictures.

Guest artist: Ethel kamwendo banda

Advance ticket : k20000
Contact details
Carolyn Banda 0993859014
Maxwell Billy
0884429059

10/07/2024

Mwangolowatu basi opanda ka Good night olo kosochera. Asisi kodi Madzi wa mukumangomwa basi??
Good Night omuwonela pa Umatha.😴

10/07/2024

Pali oyimba enaake munawatuluka anthu inuyo koma tikawatchula ifeyo ikhala ngati hate 🙄

JUST A REMINDER In 2020 Phyzix released MAKOFI
10/07/2024

JUST A REMINDER

In 2020 Phyzix released MAKOFI

10/07/2024

Kuyenda ndi mkazi okwatiwa imeneyo ndi ngozi utha kufa mwachangu koma Kuyenda ndi mamuna okwatila akuti palibe vuto liri lonse

Mabwana kunjaku iwowa zama Iphone zi sikweni kweni uwawona akugwilitsa ntchito ka phone k**a keypad ukuso ka Itel ,zawo ...
10/07/2024

Mabwana kunjaku iwowa zama Iphone zi sikweni kweni uwawona akugwilitsa ntchito ka phone k**a keypad ukuso ka Itel ,zawo phee matsiku nkumapita👏

Koma enanu sikuzivuta kwakeko.

Itha kukhala mphepo ya July kapena akudwalaKoma sizilibwino wachibale
10/07/2024

Itha kukhala mphepo ya July kapena akudwala

Koma sizilibwino wachibale

Happy birthday Teddy Makadi
10/07/2024

Happy birthday Teddy Makadi

10/07/2024

The Man, The Myth, The Legend Mlaka Maliro

Kombucha uja samafunika kumwa opitilira M'modzi ukakhala zoti ukupita pa stage😃

Eeeh 🙌 olo mutakhala inuyo mungakanike kupepesa apapa??
10/07/2024

Eeeh 🙌 olo mutakhala inuyo mungakanike kupepesa apapa??

10/07/2024

Akuti zinafika mpaka poti "Man Phyzo ndisiyeni musandihede, inetu ndi Pop Young. naneso ndimayimba, simunamvereko 'Mesa'?"

10/07/2024

Koma anthu ambirinu Ex mmadana naye kuposa satana bwanji🙄

_Chimakhala chili chani mukanayamikira bwenzi lanu lanyuwani mumafuna mumunyoze ex?

Nde ak**akuyamikira iweyo chifukwa ndiwanyuwani kwa iyeyo umayiwala kuti tsiku lina udzakhala EX😃

Anyways, awa amatha kuyimba awa. Villy Kay "Naiwe"

Full HD video 👇
https://youtu.be/zFwSpp7efww?si=1xrzTnY67aAtpD3t

Mwachidule mbwenu yi amanama si choncho? 🤔
10/07/2024

Mwachidule mbwenu yi amanama si choncho? 🤔

Address


Telephone

+265993926689

Website

http://www.umathadaily.com/

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Umatha Daily posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Umatha Daily:

Videos

Shortcuts

  • Address
  • Telephone
  • Alerts
  • Contact The Business
  • Videos
  • Claim ownership or report listing
  • Want your business to be the top-listed Media Company?

Share