Engin Firat Kenya head-coach post match interview after the game against Ivory coast at Bingu Stadium .
“We played mostly with local players against those competing at the highest level. If you look around, I am proud of the boys because, in the last six months, we played against the current Asian champions Qatar and won. We also nearly won against the former European champions, Russia. Against the current African champions, we deserved to win,” said Firat.
Kodi kwanuko akuti chani za Flames lero timwanso Mkaka?
MATCH ANALYSIS FROM COACH OF BURUNDI AS THE GAME VS KENYA (HARAMBE STAR) ENDS 1-1 .
FCB Nyasa Big Bullets Director of supporters Stone Mwamadi followed by Silver Strikers supporters chairperson Kingsley Malaya comments on the closure of past supporter turbulences they had.
Ma Points angati kwa Coach Patrick Mabedi?
Mabedi wati anyamata anakhutila mwansanga, atatsogola ndi zigoli ziwiri. iye anakakonda unakakhala Mtibu wa zigoli (10)
zambiri mu interview
Silver striker CEO Patrick Lonjezo Chimimba pamodzi ndi akuluakulu amasapota lero anakumana ndikukambilana ndi akukuakulu a FCB Nyasa Big Bullets ndipo apanga njila zolimbikitsa Ubale ndi chitetezo pakati pawo, zambiri mu interview
COACH ADRIANO EUSEBIO, wa Sao Tome wati a Malawi nthawi zina zimakuyendelani, koma lero sitsiku loti zikuyendeleni.
muona za Kuda..
COACH ELIAH KANANJI, "Blue Eagles nayonso ikufuna kuzigulira malo mu Super League"
COACH MABEDI kufotokoza mmene wakonzekela game ya mawa, Malawi vs Sao Tome & Principle.
COACH FRANK, Training Kids a rare sport in Malawi, roller skating.