Zamkalasi Mwathu Entertainment Media

  • Home
  • Zamkalasi Mwathu Entertainment Media

Zamkalasi Mwathu Entertainment Media Zamkalasi mwathu Entertainment is a Media Platform and Brand. Promoting
Advertising
Entertainment updates

Madness Entertainment timati mumuonetseko Sativa Madness nyimbo yi   Blasc Muzik Mw ft Dj Muller Mw. Link in Comments
22/02/2025

Madness Entertainment timati mumuonetseko Sativa Madness nyimbo yi
Blasc Muzik Mw ft Dj Muller Mw. Link in Comments

Koma mwana uyuyu eh 🙌🏾 🎥 Veda Njucci
20/02/2025

Koma mwana uyuyu eh 🙌🏾 🎥 Veda Njucci

Uyu muikeni pa list ya Oyimba omwe Akwatira Azungu. Mulamwache yoo Ali birthday lero koma Wathuyo ati mphatso apereka ma...
17/02/2025

Uyu muikeni pa list ya Oyimba omwe Akwatira Azungu. Mulamwache yoo Ali birthday lero koma Wathuyo ati mphatso apereka madzulo 5pm.

Dedication song to his Girlfriend "LoLo" 🎬
Lunna kajuwe

Tayendedwa pansi chifukwa Sizoonayi. Emmie Deebo anthu ma group mu Ali mafunso mbwee!!!🙌🏾
16/02/2025

Tayendedwa pansi chifukwa Sizoonayi. Emmie Deebo anthu ma group mu Ali mafunso mbwee!!!🙌🏾

16/02/2025

Azibambo Ambiri omwe Ali ku page ya Morale The Rapper ndima blesser 😂🙌🏾💔

Congratulations to Chiksy  His Song "Ku Lilongwe" hit 1 Million Views on YouTube. 🎬📸
12/02/2025

Congratulations to Chiksy His Song "Ku Lilongwe" hit 1 Million Views on YouTube. 🎬📸

06/02/2025

Iwe ukuwerengawe, lero upeza chibwezi 😂🙌🏾💔

2023_2024 Malawi 🇲🇼 Music industry was Blessed with These Stars:JetuFada MotiAbambo BunneyShano IndexMalimba MusicAbebu ...
05/02/2025

2023_2024 Malawi 🇲🇼 Music industry was Blessed with These Stars:
Jetu
Fada Moti
Abambo Bunney
Shano Index
Malimba Music
Abebu Music (Chain oh Abebu and Fresh Don Abebu)
Ellan Monjeza
Lady Aika
Aidfest Madness
Kineo Madness
Joe Ikon Madness
Taimon Tipa
Chiksy
Emmie Deebo

Kungoyamba Gospel Chilichonse Chinasintha. Ma deal mbweeee alemekeze Yehova.🙏Waxy Kay
28/01/2025

Kungoyamba Gospel Chilichonse Chinasintha. Ma deal mbweeee alemekeze Yehova.🙏

Waxy Kay

Happy Sunday y'all.Coming Soon📌Mama Bishop Mary Kapenga Feat WWaxy KayKWaxy Kay
19/01/2025

Happy Sunday y'all.
Coming Soon📌

Mama Bishop Mary Kapenga Feat WWaxy KayKWaxy Kay

17/01/2025

Plan yanga ya 2025 ndikuvotera "Chakwera" kumapita ku Jonz zanga Chete 😂🙌🏾💔

11/01/2025

Pano Kungomva Mawu oti "Boma ndilomweli" simene kumafookeramo 😞💔🙌🏾.

10/01/2025

Pa Birthday yake nnamuvungila 50 pin, pa yanga anangondiposta ati "A king was born",.. Carol ufumuwo anandipasa ndi ambuyako??

Kodi Muona Ngati Ras yu Akulakwitsa pati?? Kupulumutsa moyo Wa Legend Paul Banda
09/01/2025

Kodi Muona Ngati Ras yu Akulakwitsa pati?? Kupulumutsa moyo Wa Legend Paul Banda

Happy New and Happy birthday Mic Mash 🎂🥳🧨New Project on 31 January. "To The Moon & Back"
03/01/2025

Happy New and Happy birthday Mic Mash 🎂🥳🧨

New Project on 31 January. "To The Moon & Back"

Bachelor of Arts Ep on 27 December📌Malinga Mafia
20/12/2024

Bachelor of Arts Ep on 27 December📌Malinga Mafia

Uyuuu ndi Aphillo Ofcoz kuchokera ku Bangwe. Ndi mwana amene Ali behind FADA Motionist brand. Kwa omwe mamvera nyimbo za...
17/12/2024

Uyuuu ndi Aphillo Ofcoz kuchokera ku Bangwe. Ndi mwana amene Ali behind FADA Motionist brand. Kwa omwe mamvera nyimbo za fada , mumamveka mawu Ena ake a Bass. Ndipo mawuwo amayika ndi mwanayi Zina mwanyimbo zomwe anayimbamo ndi:
Mudyera
M'sundithawe
2+5 kuphatikizaponso ka slogan kaja amati "Ndine mwana wa Mayi"

Kupatulapo kuyimba nyimbo za Fada iyeyu Amayimbanso nyimbo zake ndipo Ali nazo zingapo :
Madzi pang'ono
Mwana wanga ndi zina ndipo posachedwapa akhala akutulutsa Ina "Usa" yomwe akuti itha kuvutanso...

Behind everry man success kuli Anthu omwe amathandiza munthu uja musamangoona the fruits..

We reached 5.4k people in Last 7 days. Thank you all for your support 🙏🙏Let's keep on following this page 🙏
13/12/2024

We reached 5.4k people in Last 7 days. Thank you all for your support 🙏🙏

Let's keep on following this page 🙏

Address


Telephone

+265888846324

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Zamkalasi Mwathu Entertainment Media posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Zamkalasi Mwathu Entertainment Media:

Shortcuts

  • Address
  • Telephone
  • Alerts
  • Contact The Business
  • Claim ownership or report listing
  • Want your business to be the top-listed Media Company?

Share