Amar Chris TYM

Amar Chris TYM Official page for Amar chris the producer, songwriter, singer,

11/11/2023

Mfumu ndiyamwano iyi sifuna kusintha Mfumu Hyphen 🤣🤣🤣🤣

08/11/2023

Sean Morgan Official ndiyemwe zake nditha kuyankhula mosabisa Kuti adha awa Ali ndi luso keep on 🔥🔥 mulungu azipitiliza kusunga talent yako...

Mukapeza time muveleko nyimbo Za mbaleyu zakale ndizapano zomwe mupeza ka answer kafuso lomwe simunazifusepo....
💕💕💕😒🔥🔥

01/08/2023

nawo a Tremour aaaa 😭😭😭😭😭😭

30/07/2023

Zosayenda zinthu zake 😭😭💔
Luso likungokhala ngati ndi njila okumanilana ndi IFA 😭😭😭😭

TremourTremouri_do_it_for_all_of_us

27/07/2023

we need old Madness Entertainment plz DonZo ndi Charisma Madness mumabebetsa ndikutha ....

24/07/2023

DonZo wafika kale Charisma Madness tiyeni konze wamtendele 🔥🎶

11/07/2023

Giboh Pearson Phalombe Musik ndiwoimba yekha mmodzi Ku konse 🔥😂😂

11/07/2023

kodi Dr Manganya mwasanduka a coach? Tikudabwa nazotu 😂😂😂



10/07/2023

mmalawi muno mulibe oyimba owoneka bwino kuposela Gibo Gift Lantosi 💗🔥

Zimangovuta chamba alumewa 😂😂😂😂

13/06/2023

Ndikufuna kunenepa ndiye ndizing'ophaka grace...🔥
Omukonda ndiomutsata MMartse FoundationFMartse Foundationtamalizitsani tione

13/06/2023

Ndiyamika wammwamba poti oyipa walephera ....🔥
Omutsata ndiomukonda MMwanietamalizitsani 😂😂

13/06/2023

Wapalamula kudambwe ....🔥
Omudziwa CCharisma MadnessMCharisma Madnesstiyeni timalizitse 😂😂

13/06/2023

ndimapha nyimbo rest in peace 🔥 omukonda GGwambatiyeni timalizitse 😂😂😂

02/06/2023

aiwe 😂

24/05/2023

Nkhani ndiya Martse Foundation basi zinazo miyezi ukubwerayi 😂😧

eti eti koma time ndikafiti 😂😂😂
24/05/2023

eti eti koma time ndikafiti 😂😂😂

2009 eeeeeh only legends will understand

24/05/2023

Pamapeto pake kundicha stage master 🔥
Fact koma 👀😂 ChaCharisma MadnessdCharisma Madnessi_do_it_for_all_of_us

Address

Mzuzu
123

Telephone

+265880262097

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Amar Chris TYM posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category