Mighty Wanderers Football Club Mw

Mighty Wanderers Football Club Mw Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Mighty Wanderers Football Club Mw, Digital creator, Lilongwe.

28/09/2024

Bangwe imamphwekera Neba emwe uja ife si size yake.

Ngati mukufuna team dziwani kuti team ndi.........

28/09/2024

Bangwe taking their 4th penalty

And he misses

We are through to Semi Finals

Thole Saved Two Penalties

๐Ÿ’™๐Ÿ’™๐Ÿ’™๐Ÿ’™๐Ÿ’™๐Ÿ’™๐Ÿ’™๐Ÿ’™๐Ÿ’™๐Ÿ’™๐Ÿ’™๐Ÿ’™

28/09/2024

Inthera ku ma penalty

28/09/2024

BANGWE 1-0 MIGHTY

Komabe team mukuidziwa

28/09/2024

Big shout out to my newest top fans! Frank Junior Kalikwembe, Raurence Chewa, Sido John, Paulo Costa Armando, Maxy Wa Makupe Junior, Mtayamanja Kevia Kelvin, Nepear Nkhwali, Victor Kapakasa, Sฤซรฑรตyรฃ Mร rtรฎรฑ, Chisomo Banyirah, Andrew Bob, Chikond Wa Nkhoma, Chisomo Chisi, Lordwell Kanjatika, James Boman

25/09/2024

Lelo mwadzukila kuti inuyo?

๐Ÿ”ต๐Ÿ”ต๐Ÿ”ต๐Ÿ”ต๐Ÿ”ต๐Ÿ”ต

Team ndi yomweyiNanga kulinso ina komwe kuli zabwino ngati?
21/09/2024

Team ndi yomweyi

Nanga kulinso ina komwe kuli zabwino ngati?

21/09/2024

Manoma 10:0 Baka

Koma chifukwa chani akukwiya ndi a team ina yomwe sikusewera nawo lelo?

21/09/2024

Ife timamenya, ndati timaumbuza, eya timaswa..........

Munkhoza kuonjezera

21/09/2024

Kaya mukumva mmene zikuyendera kuseliku?
Chifukwa Tikanena zizimveka ngati matama.


Team ndi yomweyi

21/09/2024

Game Day
TNM Super League
Mighty vs Baka City
Kamuzu stadium
2:30PM
3pin Open stand

MANOMA!!! ๐Ÿ˜ Masewero athu otsatira tidzasewera loweruka lino pa 21st September,2024 ndi team ya BAKA CITY mu TNM SUPER L...
20/09/2024

MANOMA!!! ๐Ÿ˜

Masewero athu otsatira tidzasewera loweruka lino pa 21st September,2024 ndi team ya BAKA CITY mu TNM SUPER LEAGUE pa Kamuzu stadium.

Masewero ofunikira kwambiri omwe atadzayambe nthawi ya 2:30 masana.

Mitengo yolowera pa chipata ili motere:

-K3000 open stand.
-K4000 MBC stand.
-K5000 Covered stand.
-K8000 V.I.P stand.

Tiyeni tiyeni MANOMA tikawapatse molaro anyamata athu ๐Ÿ”ฅ

Team ndi yomweyi....

19/09/2024

Nonse mumati Dikilani Neba Nkumadzulo....

Kodi tizidikilabe or tinkhoza kugona?

19/09/2024

Tingoti aidziwa bangwe...

19/09/2024

Ati Bangwe ndi team ya ana komatu si mmene kulili.

Neba tiyankhuleni......

19/09/2024

Tnm Super league titenga....

Ana achepa

Zikayenda bwino awa ndima plan apa likoma Island..... iyi ndi team yoona patali.Team ndi yomweyi basi.
16/09/2024

Zikayenda bwino awa ndima plan apa likoma Island..... iyi ndi team yoona patali.

Team ndi yomweyi basi.

Basi zimachitika.Komabe team ndi yomweyi.
09/09/2024

Basi zimachitika.

Komabe team ndi yomweyi.

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mighty Wanderers Football Club Mw posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Videos

Share