DJ Wadu

DJ Wadu Giving the best not the worst

06/08/2024

Wina akuona ngti Airtel yamubwezera ngongole guliramo ma units uwone zomwe ikuchite

01/04/2024

Chibelekelo ft Joseph Nkasa
Pa Channel O
Ngini ilidibho
Mnyamata wa Mchape

Kametedwe kake kameneka Ku Malawi kuno sakhoza kumangoti oba chimanga aja ndamenewa
31/03/2024

Kametedwe kake kameneka
Ku Malawi kuno sakhoza kumangoti oba chimanga aja ndamenewa

Anthu adera amapanga izi
18/03/2024

Anthu adera amapanga izi

22/02/2024

Ambuye tichitileni chifundo
Pamene timalakwitsa muzitikhululukira
Ndife zolengedwa zanu tikupempha mvula osati dzuwa monga zililmu
Tikudziwa kti simulakwidza
Koma tiganizilenkoni 🙏

Mmera wAbwino uja wayamba kunyala 😥😢

Dzina lanu lizamekezedwa munthawi zonse ndi nthawi zosatha

20/02/2024

Kukanika kugona chifukwa chani

Awamanga kamba konamiza anthu kti ndi  azilangizi NEEF
08/02/2024

Awamanga kamba konamiza anthu kti ndi azilangizi NEEF

08/02/2024

Kodi ndi chifukwa chani anthu ambiri amene ali ndi dazi amakonda kumeneta mpala

Penapanitu tidziwe nawo

07/02/2024

Mpira ndi choncho samawina onse

usku wa bwin

30/01/2024

Muzii thokoza kampani yopanga soya pisezi ija ikusamala aMalawi ambri

14/01/2024

Mbali yakuno Alhamdullillah🙏🙏🙏
Tadzuka bwino kaya inu
mwadzuka bwanji kumeneko

11/01/2024

Ngti mmpingo ukukanika kubweza ngongole ndiye ine ndi ndani
kti ndikubwenzere ngongole

18/12/2023

Mukapeza Mpata masana ngti ano muziayendelakonso anzanu aja amapanga post zinthuzi ngti Ali ku London
Muzaone

Muzakhumudwa ndithu
Akukhala osadya
kwa masiku angapo

04/11/2023

Nthawi yolima yafika anthu
Muyambepo kukwatrana
Muzidzakanana munyengo yokolora

Mwaswera bwanji???
nkhumaliro yanu ikuenda

Ngti simunadye osataya mtima

13/10/2023

Zili bwino kamba koti lero kwazizira

09/10/2023

Mukapeza Mpata muzimukumbuka Mulungu

Address

Paul Kagame
Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when DJ Wadu posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category