Mlaliki Steven Rudd wati palibe m'dindo wankulu kuposa m'zake pa Mpingo.
M'mau ake wati abusa, atumiki, komaso alaliki onse ntchito yawo ndi imodzi kotero sipafunikaso kukhala kagulu kena kapadela komwe katha kumatsogolera Mpingo.
"Nkolakwika kukhala ndi kagulu koyendesa Mpingo chifukwa Mpingo ulionse ndi oima pa okha" anatero Steven Rudd.
Maphunzilo omwe ndi amasiku 10 anakali mkati ku Capital City Motel ku Lilongwe.
#within
Alaliki ochuluka a Mpingo wa a Khristu akuoneka achidwi pomwe Maphunziro a Baibulo ali mkati ku Capital City Motel mu m'zinda wa Lilongwe.
Ophunzitsa pa maphunzirowa ndi Mlaliki Steven Rudd ochokera m'dziko la Canada.
#within
S Bizzo has finally recorded a song dubbed Teteleli which is expected to be released soon.
He has featured Witny in the song.
Behind the production is Nefter and Witny.
#within
Pomwe muli pa Chibwezi nkokoma kudziwa umo momwe matupi anu alili kuopa kupatsilana matenda opatsilana pogonana.
Gulu la FYLET likutiphunzitsa kudzera mu Sewero..
#within
Gulu la zisudzo la FYLET kuphunzitsa ana a Sukulu pa Kaliyeka Community Day Secondary School.
Ndi luso ndi zotheka kusintha kaganizidwe kolakwika pakati pa anthu πͺ
#within
POKA POKA Video to be released on Thursday π₯
Major General khalen the best rapper wadza mwachabe π
#within
FRIDAY BARZ πΆ
Major General khalen the best rapper on Friday Barz π
Ioneleni yonse potsatila YouTube link mu Comment Box ??
#Within
Okondedwa ma DJ
Ife a Within the Ghetto (WTG) timajambulaso ma Samples apamwamba m'mene inu eni mukufunila pa Mitengo yozizila ya Ghetto.
Tipezeni ku WhatsApp or kuimba tipange business ya Smart :
C / W : 0884987221 / 0994689540
#Within
FRIDAY BARZ β¨
A sting Freestyle by S Bizzo
3rd May 2024
Follow the YouTube link in the Comment Box to watch a full Freestyle.
#Within
GHETTO STAR ADYE MONEY π°
WTG Freestyle Challenge Epi 2
Uyu ndi Kay Star Muwasi from Zomba, Ikakhala ndi ma likes ochuluka pofika pa 3 March 2024 izakhala yapambana.
#within
GHETTO STAR ADYE MONEY π°
WTG Freestyle Challenge Epi 2
Uyu ndi De Wintoz from Lilongwe , Airwing. Ikakhala ndi ma likes ochuluka pofika pa 3 March 2024 izakhala yapambana.
#within