27/03/2020
Lyric yapamwamba nyimboso yapamwamba
After Dj's from various radio stations rejected this latest single by RONIK ZGAD and Macelba for being political, he decided drop it anyway https://mikozinet.com/music-ronik-zgad-x-macelba-pempho/
INTRO
ayaya!
Ayayayayaya
Zgad X2
Macelba X2
Minyama izathe
Zathe!!
Koma flames Njema
Njema!!
Mavuto azathe
Zathe!!
Koma Ghetto Njema
Njema!!
Verse 1:ZGAD
God I ain't prayed for days
Copy cutting my friends
And jesus peace off my lenz
Dzuloso nnali Chez
Koma ndungofuna verse
Idzapheletu matembelelo onse a flames
Ndikafandi imodzi bet isamakhale flames
Flames ndi nyesti
Iwe ghetto ndi nyetsi
Koma ipatseni getsi
Make us hella rich Lord!!
Isamavutitse bill getsi
Mulungu atate
Nayo college isazathe
Koma mayeso azathe
Azatenge degree nfana wa party after party
Mtima wasatana ife toto
Uponyeni pamoto
Satana azipsa mtima
Nfuse 'celba,
ngat photo
Malawi anangoima
Ghetto yuthi alimomo
Angokhalila kuthima
Sley queen ndi smoko
Akakhala amangoima
like
Who got the keys to mi Bima
IMA!
HOOK
Minyama izathe
Zathe!!
Koma flames Njema
Njema!!
Mavuto azathe
Zathe!!
Koma Ghetto Njema
MBUYE ndi PEMPHO
Devil NJEMA
K*k NJEMA ! X 2
Verse 2:MACELBA
nsanje izathe
Koma mayi Malawi
asazathe mpaka day imene amalawi
azazindikile nsanje simanga mudzi
Azathe maudani ose opasula mudzi
Ghetto isazathe
Ghetto singathe
Uzathe ndiumphawi opangitsa mabanja athe
Timangokhala pompobe chonchobe!
Kukhoma zimisonkhobe tilipamotobe!
G anthu amakhala muchi Den
Tchalitchi lero anachilowestaso gain
Amayenda mwanseli ndi amayi anvano
Apatsaso pathupi nkazi wasoprano
Amayi Busa amakhalila misonzi
Pemphero langa ambuye ndupemphako chimodzi
Mipingo isazathe
Mawu anu sangathe
Koma aneneri onyenga onse muwakanthe!
Back to chorus X2