Pabwalo sweet stories & Addvitisement

Pabwalo sweet stories & Addvitisement it's where you can have sweet stories and advertising what you have

My Mother's heartShort story by James George mulengaDon't forget to like and follow this page for more storiesSceen 1Lov...
27/02/2024

My Mother's heart

Short story by James George mulenga

Don't forget to like and follow this page for more stories

Sceen 1

Love is blind

Ooooo nono no this is an fair!!! God why you allowed this to happen?

Joe my son pleas come and eat since morning you didn't eat anything what is bothering you ?

Joe ; mama it's getu mama she is dieng at the hospital ?
Mama:what happening to your fiance
Joe ; mama I told you that she had deficult with her heart,

Mama : am sory my son,don't wory she will be fine come and eat we save a miracle God she will be fine
Joe ; mama how can I eat while my heart is not feeling well ,yesterday the doctor said that she remain with 48 hours if there will be nobody to donate a heart to her I will lose her ,
Mama : ooo my son am sorry I didn't know that it reach to that mess eash

Joe ; mama ooo no if getu will die and I will die with her I don't want to lose her
Look mama what will I be if I lose her she is my happiness my everything oo no God have pity on me pleas.

Mama ; my son don't wory come and eat first I will go with you to the hospital oky I know what to do oky

My only son ,akufuna kudzipha chifukwa Cha ms*kanayu zoona kutheka amamukonda kwambiri no ndidamuvutikila mwanayu kuti abadwe akule ndye ndingomuluza mopheka chonchi no koma ndimupangile chinthu chomwe azanyadile moyo wake wonse akazamandikumbukila .

Tidanyamuka ine ndimwana wanga joe ulendo wakuchipatala ku central hospital.

Joe don't wory getu will not die ndipo ukamachoka kuno uzipita naye limodzi oky

Joe ; are you sure mamu ,I really trust you so mulch

Mdamuyangana mwana wanga kumwetulila kwake kudandukumbutsa nthawi imene atangobadwa kumene adamwetulila , ndidaziyankhulila ndekha ndukapeleka mtima wanga ngati msembe kuchimwemwe Cha mwana wanga ndi mpongozi wanga wa msigolo .

Ipitilile nkhaniyi Kodi kapena silibwino ma comment anu ndamene apangitse nkhaniyi kupitilila

∆∆∆∆∆∆∆∆∆ TRUE LOVER∆∆∆∆∆∆∆¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶∆∆∆∆∆∆∆¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶A short story by James m...
26/01/2024

∆∆∆∆∆∆∆∆∆ TRUE LOVER∆∆∆∆∆∆∆
¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶∆∆∆∆∆∆∆¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶

A short story by James mulenga

Dont forget to like this page for more stories

Sceen 1

Mphuto yakalulu idakula mtazaoneni
...................................I love u so much
................................Box Ur my heart...................................Love is two pple

Dear my Love phwedo

Ndalemba kalatayi pofuna kukudziwitsa momwe ndikumvela,komanso kukudziwitsa chona chokhachoka maka pa chophweteka chomwe lelo lino dziko lidandikamo kuphatikizapo iweo .

Phwedo ineo sindine hule monga mmene dziko likuyankhulila komano zonsezi zidachitika chifukwa ndimakukonda kwambiri ndipo sindikafuna kukuluza.

My love mmene ukadwala muja nthenda ya ipsyo ija zimafunika ndalama yoti iweo upitile kuchipatala chakunja ndukalandila chithandizo komano palibe ndi mmodzi yemwe amaonetsa kuti andithandiza kuyambila abale ako komanso omwe umati ndi anzako apamtima onse amangoyangana mkumadikila infayako izitu zikandiphweteka s*ku ndi s*ku ndipo ndimakhetsa nazo misonzi mpaka mdayamba kusakasaka njila yoti ndipulumutsile moyo wako koma palibe chimathandiza kufikila pamene mdakumana ndi mponda matiki wina amene adandiuza kuti ndikagona naye andipasa ndalamazo .

Ndye popeza mdasowa mtengo wogwila ndidalolela kugona naye popeza Kwa ine padalibe chopambana kuposa moyo wako .

Pepani kuti ndinakubisila pokuza kuti ndalama yakuchipatala adandipatsa ndi ankolo anga ,komano zona zake mzokuti kwathunso ndife mphemvu mdyela ku mthiko palibe amene angapezeke ndi ndalama ngati imene ija.

Phwedo mkati mwanga mukuyaka moto ndikaona ngati ndibisa chinthu choipa ichi komano zidabwela pambalambanda chifukwa Cha mwana amene ndanyamulayu,pena ndimafuna nditangomwa mankhwala kuti ndikaphe kamwanaka koma ndidazizindikila kuti ndichiyembekezo chokhacho chomwe ndili nacho chomwenso chili chikumbutso changa pa chikondi changa pa iwe

Ndimakukonda phwedo kwambiri

Ndatha ine wachikondi wako Eliza

Kodi mudaesako kukwilila nthochi mu nthaka ? Nanga mutakwilila chidachitika ndichani ? Tapangani koment kapena like this...
05/01/2024

Kodi mudaesako kukwilila nthochi mu nthaka ? Nanga mutakwilila chidachitika ndichani ? Tapangani koment kapena like this page kuti mumve tsatanetsane wake!!!!

03/01/2024

KODI MWAYIMVA ?

❤️❤️❤️ ITATHA MISONZI ❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️A short story by James g mulengaDon't forget to like this page...
26/12/2023

❤️❤️❤️ ITATHA MISONZI ❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️
A short story by James g mulenga

Don't forget to like this page for more stories

Sceen 8

Ndidalowa mnyumbayi koma eee guys ndimaona ngati mwina ndafika dziko lina ,ndisaname chilichonse chimandipasa chidwi kuyangana mipando idali mnyumbayi sipamalephela kupezeka golide makapu eni eniwa nawonso adali agolide ndinganene table nayonso ndiyagolide ndinene kuti 80 % ya dzinthu zomwe zidali mnyumbayi zidali za golide ndidaziyankhulila ndekha is this a house or mparadiso?

Mwati; James wellcome to my house feel free
James; oo thanks
Mwati; glory grory?
Glory; maa am here
Mwati; Tenga chikwama ukasiye kuchipinda komwe azigona jameyi .
James umusatila glory kuti akakuonetse chipinda chako?
James;ooo thanks mwatitha
Mwati; your wellcome

Ndidauyamba ulendo wopita kuchipinda komwe ndikhale ndikugonako mopelekezedwa ndi nts*kana ameneyu glory

Glory;sir this is your room
James;ooo thanks koma sitidalonjelanetu ,moyo wabwino koma?
Glory;wabwino ndiope inu
James; wabwinonso ine dzina langa ndine James Banda iwe nanga?
Glory:monga udawamvela madam aja langa Zina ndine glory thengo ndine amene ndimasamalila nyumba ino

James;ooo nice to meet you
Glory;nice to have you in this house pakafunika chilichonse ndyekuti mundiuza.

Ndidalowa mchipinda mwangamu oo s**t Kodi mchipinda ichichi kapena nyumba ya payokha nanga chipinda mpakana kitchen,toilet mpakananso bathroom kkkk eee kuphunzila s*kutha eti! Ngizizi tiona nazo zosaona ndithu ndidagona pa bedili mkumapumula.

Joe is this true ? Are you a such kind of guy ooo you killed me am deado!!; Osandiuza zoona zoti ur HIV positive?
Joe; love am sorry you know I love you so much s*kuti sindimafuna kukuza komano kuti ndidali ndi mantha to tell you about my stutus
Love; oo no this not love udakakhala umandikonda zenizeni bwenzi utandiuzilatu koma wadikila tagonana gonana mosazitetezanso and mkudikilanso kuti ndifufunze ndekha no there is no love noonoo
Joe; baeb forgive me????

🇲🇼🇲🇼🇲🇼 THE BROKEN RING 🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼A short story by James g mulengaDon't forget to like this pag...
25/12/2023

🇲🇼🇲🇼🇲🇼 THE BROKEN RING 🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼

A short story by James g mulenga

Don't forget to like this page for more stories

Sceen 1

Hey beautiful lady ,how are you?
Eeee you bitch don't touch me , don't even try to great me !!! Don't you see that I am a fiance to the next king of this Kingdom in fact I am the next queen of this Kingdom!!
Boy; so what's wrong in greating you?
Madam; kkkk you don't see where is wrong right can you come closer?

The boy goes closer to the girl and he was badly slapped

Boy ;madam you slapped me ?
Madam; yess I slapped you ,this will always reminded you that am not of your class and in addition that am not a ordinary girl whom you should call or touch without athorisation hope you head me clearly!!!
Boy: but madam what did I do to deserve this? But do you know who I am ?
Madam:kkkkk I don't need to know who you are !!! A peasant boy like a useless infact a reckless man like you may thunder hit you

I left the place but I was so disponted is this type of the girl my father chose for me to marry,no I can't marry that wicked girl.

Is this the way she will treat our people in this village? Thanks God for revealing this before I marry her eee I wana marry a monster

Let's meet mu next part coment or like this page for more stories happy xrimas I love you o

25/12/2023

Happy happy xrimas wishing everyone a wonderful Christmas I love you o

20/12/2023

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Rhoda Mtenje Malikebu, Mayeso Afraid

❤️❤️❤️ ITATHA MISONZI ❤️❤️❤️❤️❤️❤️ ❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️A short story by James g mulengaDon't forget to like this pag...
18/12/2023

❤️❤️❤️ ITATHA MISONZI ❤️❤️❤️❤️❤️❤️ ❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️

A short story by James g mulenga

Don't forget to like this page for more stories

Sceen 7

Kuyangana magalimoti amene adali ku mpandaku sindidasimikile kuti zinthu zotelezi zingapangidwe ndi munthu wa mkadzi

Mwati: jame bwanji ukungoti maso mwamwa ngati nkhuku yoti ifuna ikile madzila?

James: mwatitha ndisaname mutu wanga wasiya kugwila ntchito apapa magalimoti onsewa Ako?

Mwati:eya ndianga ndithu
James; BMw ,hummer mpaka six dors nduze chinsisi kapena mwina unajoina pansi pa njanja eti ?
Mwati: James sisataniki ayi izizi ndikugwila kwanga ntchito molimbikika kwandipangitsa kukhala ndi izizi ,ukamakhala uziziwanso kuti mulungu amadalitsa ndipo mau amulungu amati silver Gold zonse mzake za mulungu olo Iweo utamupempha akhonza kukupatsa

James; mwatitha zomene ulinazozi akukanika amuna kukhala nazo ndye Iweo munthu wamkazi zitheka bwanji? Ukundijamitsa malingalilo anga this is too much it's beyond my expectations I think there is something beyond this!!!.

Mwati; ukuganizatu molakwika James like area on ndidakufotokozela kuti akadzi osamawayanganila pansi nawonso Ali mkuthekela kopanga zazikulu nkhani mwanayo mulimbikitseni kaya ndi maphunzilo kaya busness ndimamva chisoni kwambiri makolo ena saerekeza olo kumulipilila mwana wa mkadzi sukulu ku secondary ati ayi azakwatiwa mamuna wake ndamene azizamusamala mchifukwa chake akazi ambiri akulandila nkhanza zosiyanasiyana mmabanja kamba koti amaziwa kuti banjalo likatha sangathe kuzimilila pa okha ndye amalolelabe kukhala mu ndende ya mabanja koma sichonchoyi aliyense angathe kuboleza

James: zoonadi sukulu sithadi pongokuonani inuo mwandisatsa phunzilo lalikulu komanso zomwe mwandiuzazo zandisegula malingalilo anga ndimawawona akadzi molakwika kwambiri apapa ndazindikila madam mwatitha mulungu salakwitsadi ngozi imeneyi yandipangitsa kuti ndiziwe zambiri
Mwati; kkkkk watelo tiye tilowe mnyumba

Jame;oky fine

Ndidalowa mnyumbayi guys eee koma ya ndimaona

❤️❤️❤️❤️ ITATHA MISONZI ❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️A short story by James g mulengaDon't forget to like this page...
15/12/2023

❤️❤️❤️❤️ ITATHA MISONZI ❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️

A short story by James g mulenga

Don't forget to like this page for more stories

Sceen 6

Maso anga adaseguka moti ndidazindikila kuti ngakhale ms*kana Ali mkuthekela koboleza ndipo ndidaziyankhulila kuti nane mkazakhala ndi mwana wa mkadzi ndizamuphunzitsa nduzamulimbikitsa kuti azakhale wozidalila mwa iye yekha

Mwati ; jame sukundiuzatu kuti ndizilowela kuti? Maka ndimafuna ndiziwe kuti umakhala kuti?

Jame; mwatitha ineo ndisakubisile ndilibe kokhala moti nthawi umandigunda ija zidali kuti ndasamusidwa ndi alandioad mnyumba yomwe ndimakhala moti sindikuziwa koti ndiloweleyi!!
Mwati; eee jame akusamutsa bwanji simumalipila ndalama ya lenti?

Jame;eya chimenechi mchifukwa chomwe anditulutsila moti ndilibe kokhalayi!!

Mwati; Owo Kodi ndinu atambwali aja eti othawa kupeleka lenti?

James;no sine tambwaliyi,vuto ndiloti nyengo yomwe ndikudutsa ndiyolhweteka kwambiri,ntchito yanga chinditheni miyezi six yapitayo mpaka pano sindidapeze ntchito ina ayi!!

Mwati:mezi ingati? Mpaka half chaka osapeza ntchito
Jame; ndukuza mwatitha moti mdakwatila mpaka mkadzi wanga adandisiya ndipo adatengana ndi munthu wina chifukwa Cha umphawi sindikuziwa kuti chikundisata ndichani maka maka?!!

Mwati: oo no am sorry for that eee zomvesa chisoni Kodi uli ndimaphunzilo anji?
Jame; ineo ndidapanga za utolankhani pa mij

Mwati: moti uli ndi tsamba la utolankhani?

Jame:;eya lili msaka langa la zovala ndalembela ma radio ndi ma television station mmabungwe koma ndithu kuli zii palibe chiseko chomwe chikundisegukila

Mwatitha::pepa kwambiri komano usadele nkhawa mulungu ndiwadongosolo toyeko ukakhale kae kunyumba kwanga Kwa mas*ku angapo ndiona kuti ndikuika pati kachikenanso pepa kamba ka banja lako !!!

James; ooo dzikomo kwambiri ambuye akudaliseni pachimenechi

Mwati; sukuyenela kuthokoza jame mzochepa izi.

Ndidafika kunyumba Kwa mwatitha eeeee guys sinyumba wamba ndi nyumba ya self container kuyangana magalimoti adali k

❤️❤️❤️ ITATHA MISONZI ❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️A short story by James g mulengaDon't forget to like this page...
15/12/2023

❤️❤️❤️ ITATHA MISONZI ❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️

A short story by James g mulenga

Don't forget to like this page for more stories

Sceen 5

Mwati; James masuka usachite kumangikayi chonchiyi ngati uli muchitokosi chapolice kapena ndukuopsa? Kapena nduwoneka ngati mkango? Khala bwinobwino!!
Jame; oky madamu
Mwati; zamadamuzo ayi mesa ndakuza dzina langa kuti ndine mwatitha?
Jame;eya komabe mdaenela kukupatsani ulemu kutheka ndinu mkadzi wa bwana
Mwati: kkkkkk jame moti ndikuoneka ngati ndili pa banja ineo ?
James; eya nanga galimoti yodula ngati imeneyi Iweo ungaipeze bwanji eee simamuna wambatu ameneyu adagwilako ntchito mboma?
Mwati: James usandiseketse Kodi mkadzi aliyense akuyendetsa galimoti umaganiza kuti ndiyamunake?
Jame;eya
Mwati: no jame kuli akadzi oti Ali pa ntchito amazipangila okha zinthu mwinanso kuposa mamuna!!!

James;Owo zimenezo mzosatheka mwina Kwa mkadzi oti adabadwila banja lolemelatu !!!
Mwati: no jame like ineo makolo anga ndi ovutika komano ndimathokodza kuti adandiphunzitsa mochepekedwa momwemo mpaka mdamalidza mwachisomo mdapeza ntchito ku bank komanso ndili ndi ma company a security komanso ya ma cleaner ndilinso ndi mashop omwe ndimagulitsamo dzinthu zosiyanasiyana.
James; eee moti zonsezo Iweo wekha ?
Mwati:eya ndekha ndilibenso mamunayu mkazi angathe kuchita bwino bola osaziyanganila pansi
Jame:eeesh moti galimotiyi udagula wekha?
Mwati;eya ndimodzi mwagalimoto zanga imeneyi
Jame; kutanthauza ulinso ndi magalimoti ena?
Mwati;ndili ndi ambiri anga okha okwela alipo ten ndye ndili ndi ena amene amakwela ogwila ntchito kumakampani anga mdaiwalanso ndili ndi company imenenso imabweleketsa galimoto kumenekoko galimoti ya mtundu uliwonse ukaipeza!!

Atangofotokoza zimenezi ndisaname zidandizizilitsa nkhongono mkadzi zoona kupanga izizi Kwa ine akadzi ndimatenga kukhala ofoka maka kuti adangopangidwa kuti akhale osamala pakhomo mwanjila ina mkadzi ndi odalila basi koma apa matso anga aseguka ndazindikila kuti mkazinso Ali mkuthek

❤️❤️❤️ ITATHA MISONZI ❤️❤️❤️❤️A short story by j mulengaDon't forget to like this page for more storiesSceen 4At the hos...
13/12/2023

❤️❤️❤️ ITATHA MISONZI ❤️❤️❤️❤️

A short story by j mulenga

Don't forget to like this page for more stories

Sceen 4

At the hospital

Hey hey eey Kodi ndilikuti kuno? Eeeeeh wina andiuze kuti ndabwela bwanji kuno ine?!!
Chikwama changa chilikuti Kodi?

Eeehe achimwene dekhani ,kuno muli kuno mkuchipatala !!!

Ndinu ndani Kodi eeeh?

Achimwene ineyo ndine nurse amene ndakhala ndukuthandizani ,mwabwela kunoko ola lapitalo mudachita ngozi mwagundidwa ndigalimoti!!!

Madam can you come in wasisimuka apapa
Madam: ooo may God be praised
Mchim: a nurse ndindaninso awawa?
Nurse. : Madam ayankheni nokha?
Madam: ineo ndine mwatitha njovu
Ndine amene ndinakugunda
Inu dzina ndindani?
Achim: ine dzina langa ndine James
Banda, eeesh mutu wanga ine
Mwatitha:oo pepa kuti ndinakugunda
James it was not my fault ku
ngoti ndimathamangila ku
Office mdali ndi meeting pe
Pani kwambiri!!!
James: osadandaula adona ngozi Sako
Nzekela
Mwatitha: Kodi a nurse tatiuzani zotsa
tila zakupima kwanu alibwa
nji jameyi?
Nurse: chiwalo chilichonse chilibwino
Pa thupi la Jamesyu kungoti ada
Komoka chifukwa chakuzizimuka
Kwa ubongo wake komanso kume
Nyeseka kwa mutu wake !!!
Mwati: kutanthauza kuti alibwinonwino
Nurse: eya mzoti tingomupatsa mankh
wala ochepetsa ululu kuti azika
Mwa basi
Mwati: aaa ambuye alemekezeke

Tidatuluka mchipatala ,nkhawanso zidandizela abale ndikuthokoza mulungu Ndachita ngozi koma sindidavulale komano apa ndilowelano kuti ndimalakalaka kuti bola mdakavulala kuti mwina ndikhaleko mchipatalamu kwamas*ku uku ndikuona mapulani ena koma apa ndingovomeleza basi

James kwela ndikakusiye ndukhulupila sungathe kuyenda ndimmene ulilimu
Jame: okoky thanks

Ndidakwela mgalimoti ya mwana kuwalayi koma akuti akandisiye akandisiya pati kaya ndikas*ka palipon

09/12/2023

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Chimwemwe Frackson, Robert Ebenezer Banda, Malikebu Blessings Isaac, George J Mulenga

04/12/2023
❤️❤️❤️ ITATHA MISONZI ❤️❤️❤️❤️  A short story by James mulenga❤️❤️Don't forget like this page for❤️❤️❤️❤️❤️❤️More storie...
03/12/2023

❤️❤️❤️ ITATHA MISONZI ❤️❤️❤️❤️
A short story by James mulenga

❤️❤️Don't forget like this page for❤️❤️❤️❤️❤️❤️More stories ❤️❤️❤️❤️

Sceen 3

Ikakuonadi litsilo mvula s*kata, mopanda chisoni alandioad aja adanditulusiladi panja katundu wanga apa ndisaname ndidagwila njakata ,ndidasowa mtengo wogwila Nawo ana ndi azimayi adali kiseka monyokodola kunetsa ndinedi chisilu, apa zilingati kubaidwa mumtima ndi mmutu momwe mkadzi wandithawa pambali pachimenechi alandioad anditulutsa mnyumba !!! .

Komano ndilowela kuti ? Ndilibe mbale kuno zindithela bwanji? Komanso ndikati ndikhale pano aliyense azingoneikamba, no I need to go,but where ?I don't know but let's gooo.

Ndidauyamba ulendo wongoziyendela tsaka la zovala zanga mmanja osaziwa kuti ndupita kuti, mutu wanga umalemela ngati ndanyamula katundu wolemetsa kwambiri chifukwa chamaganizo amene ndidali nawo mafunso nawo adali phwilikiti ,Kodi chikundiona ndichani ine? Kapena ndikulozedwa ? Tsoka kapena? Nanga ambuye kumwambako mdakulakwilani chani to deserve this?.

Pipipipipiiiiii!!!!!poopopo!!!!!po!!!
Khuuu!!!!!!!!!

Amayo ine mayo ine mayo ine mutu wanga inee inee. Mhumhuumhuu

Abale chonde ndithandizeni ndinyamule nyamatayi timulowetse mgalimoti ndamugunda mwangozi !!o my God protect this boss don't allow him to die ....................................................let's meet mu next sceen tione kutizitha bwanji

Don't forget to like and follow this page for more stories,makoment anunso amatipasa energy

Love you all

❤️❤️❤️ ITATHA MISONZI ❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️Sceen 2Misonzi idali ikus*ka mmatso anga ngati madzi amvula ya...
03/12/2023

❤️❤️❤️ ITATHA MISONZI ❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️
Sceen 2

Misonzi idali ikus*ka mmatso anga ngati madzi amvula ya mkuntho , Kwa amene adakhumudwitsidwapo ankhonza kumvesesa mmene ndimamvela ,kunenetsa mzopatsa manyazi maka mkadzi kukupanga zotelozi!!😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭

Googogo!!!!gogogo!!!odidi kuno!!!!!

Eeee lowani!!!
Kodi ndalandload? Ndakulandilani mukhonza kukhala pepani kuti tilebe mipando!!

Landlord: sindikukhalatu ine pano nda
Bwela kuzakutulutsani nyum
ba muno mukuzalowa munt
hu.
Bambo. :Bambo wanga chonde ndidikil
Ilenkoni Kwa mwezi okhawu n
dilongosola za ndalama yanu
Please
Landlord: Kodi ndi mezi ingati wakhala
Ukundiuza kuti ulongosola?
Uno ndi mwezi wa 6 usakupe
Leka renti ndye unowu ndiwa
Mdalitso kapena? Kuti ukwa
nilitse nthabwala zakozo?
Bambo : chonde chonde ndimveseseni
Ndilibe koti ndingakhale mwe
Zi unowu ndiyesesa kuti ndik
upaseni ndalama yonse ikak
anika yonse koma half yokha
Sindilephela kukupasani?!!?
Landlord: Ineotu sindili pano kumvesel
a nthano zakozo lelo ukutulu
Ka nyumba yanga ino simda
Mangile basary kuti anthu a
Azingokhalamo ulele ndi bus
ness imeneyi
Bambo aju: ndikumvesesa komano s*k
uti mkufunayi ineo nyengo
Zomwe ndudusa mzomwe
Zundipamgitsa chonde ndit
handizeni bambo anga ndag
wada?
Landlord: ndikuti tulukani pompano NY
Umba yanga ino mwina chifu
Kwa ndikungonena nditango
khala eti dikila ndikutulutsile
Tinyangwita takoti panja za u
siru
Ikakuona litsilo mvula s*kata

Address

Lilongwe

Telephone

+265995994024

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Pabwalo sweet stories & Addvitisement posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share