02/12/2024
CHIDZIWITSO
kwa ma customer nonse komanso azanga . Dziwani izi Emm Sam Studio yasamukira pa Mchinji near Manda a Phwetekele area 36.
kungofika pamanda paja ndiyakhuleni kapena fusani k*ti ndimafuna pa Mchinji kma ngat mwafika pa Mandapo ndek*t mwandipeza coz tawandikana nawo kwambili tili pomwe ankapangira Yashie kale kale paja nyumba yakeso yomweyo .
kwa Omwe simukuvetsetsa kapena simupadziwa ndiyimbileni
Studio tizatsegula Mawa 2 :30 pm