Malume

Malume Platform for upcoming artists to grow their dreams

15/06/2024

Koma oyimba uyu Pop Mario ee zambiri mukambe ndinu 😂🙌

13/05/2024

EP RELEASE PROGRAM

• EP yonse titulutsa pa 26 mwezi Uno May lomwe lizakhale Sunday.

•Pa tsikuli kuzakhala Ka Studio listening Party plus Braai Ku Studio kwa Frëßh Çq /CQ.

•Bring a bottle ngati mukufuna muzakhale mkati🤗.

•Chomaliza kuti muzakhale nayo EP imeneyi zapangeni older ndi ndalama yosachepela K500 koma ngati mungapeleke kuposela pamenepo ndinu ololedwa kutero, izi zili chontcho pofuna kuthandiza mwina ndi mwina momwe project yalowetsa.

•Ma artist ndi mulingo wa nyimbo zomwe zili mu EP zo zidziwitsidwa p***a pa 17 Friday lubwelali.

fans can't wait to share this masterpiece 🤗🍄

13/05/2024

Malume is back🤗

11/04/2024

Nde kuli mabere ena ukagwira ngati ukuseweletsa madzi mujumbo eeeh🙃

03/04/2024

When a girl is beautiful without a brain, it is her private part that suffers it the most.

Boys ndikhale pati😂🤗

Business ilimbapo apa koma😂
03/04/2024

Business ilimbapo apa koma😂

Hahahaha 😂😂😂
03/04/2024

Hahahaha 😂😂😂

Chibelekelo a.k.a Chiberie wati akutulutsa music video yake yoyamba chaka chino, 'Zindithandiza Chani' lero 7pm
03/04/2024

Chibelekelo a.k.a Chiberie wati akutulutsa music video yake yoyamba chaka chino, 'Zindithandiza Chani' lero 7pm

Ataweruka ku church anadzera ku nyumba kwa a choir master, amakawagaira nyimbo pa Bluetooth.Malume
03/04/2024

Ataweruka ku church anadzera ku nyumba kwa a choir master, amakawagaira nyimbo pa Bluetooth.

Malume

MANGOCHI ‼️Za pa Easter HolidaysKu nyanja kunabebhatu mpaka kuiwara nkuti kwa weni.Ana ama 2 pin why kumujambula mudala ...
03/04/2024

MANGOCHI ‼️

Za pa Easter Holidays
Ku nyanja kunabebhatu mpaka kuiwara nkuti kwa weni.
Ana ama 2 pin why kumujambula mudala so.

DEDZA‼️😭😭😭😭😭😭Shooting incident in Dedza along Kasumbu road has occured about 2 hours ago.Mtsikana yemwe dzina lake ndi S...
03/04/2024

DEDZA‼️

😭😭😭😭😭😭
Shooting incident in Dedza along Kasumbu road has occured about 2 hours ago.

Mtsikana yemwe dzina lake ndi Sabina wawomberedwa ndi boyfriend wake yemwe ndiwa police kenako iyeso wadziwombera ndipo onse amwalira, pakali pano matupi awo anyamulidwa kupita ku mortuary ya Dedza. More to come

Nawo ama bus uthenga ndi umenewu🙌
03/04/2024

Nawo ama bus uthenga ndi umenewu🙌

Mkalasimo  kumanga   mmutu chonchi koma mukhonza mayeso a form 4 Eli Njuchi ?
03/04/2024

Mkalasimo kumanga mmutu chonchi koma mukhonza mayeso a form 4 Eli Njuchi ?

MCHENGAUTUWA MZUZU ‼️Prophet Habakkuk wapeza chiphadzuwa chomwe posachedwapa amange naye banja.Prophet Habakkuk ndiotchu...
02/04/2024

MCHENGAUTUWA MZUZU ‼️

Prophet Habakkuk wapeza chiphadzuwa chomwe posachedwapa amange naye banja.

Prophet Habakkuk ndiotchuka kwambiri mdziko muno.
Wapeza mkazi wapeza chinthu chabwino.

Zabwino zidyedwa ndi pumbwa.

Address

Area 23 Tank
Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Malume posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Malume:

Share

Category