Social Vibes-Out

Social Vibes-Out Hot site for discussing social issues, current affairs, vacancies, relationships and things affecting the youth for development.

A group of professors were called and sat on a plane.When the doors closed and the plane is about to take off, all the p...
18/04/2024

A group of professors were called and sat on a plane.
When the doors closed and the plane is about to take off, all the professors were informed that this plane is made by their students. Then all the professors rush toward the plane doors, trying to escape and survive on their own with exception of One professor remain seated with so much confidence and calmness.
Someone's asked him why you're not escaping the plane.
Professor answer him with confidence, they are our students.
Next Question: are you sure that you taught them well?
Professor replied quietly: I'm Sure it won't fly.
๐Ÿค—๐Ÿค—

๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚

HAVE A GREAT DAY AHEAD ๐Ÿ˜ƒ๐Ÿ‘

Joseph chikuse ยฎ๏ธ

10/04/2024
07/04/2024

Ngati amakukuntha muli pa chibwezi nde kubanja zikatha bwaa?

Joy Nathu mukanasintha koma, mumapangatu host ma show mumakhala pa public, anthu azakugendanitu inu , please change your...
07/04/2024

Joy Nathu mukanasintha koma, mumapangatu host ma show mumakhala pa public, anthu azakugendanitu inu , please change your behaviour, komaso tufuna mutiuze pomwe Pali suggestion box Ku Radio 2 kwanuko, tikaponye madandauro anthu .

07/04/2024

do y'all think relationships were better back in the day ?

Full video Link in the comment box
09/01/2024

Full video Link in the comment box

08/01/2024

'DISCIPLES: The Cult of TB Joshua'

๐Ÿ“ฝ๏ธ Watch the new three-part BBC documentary series from the award-winning investigations team here: https://bbc.in/3SbvEf6

๐ŸŽง Listen to the new nine-part World of Secrets podcast 'The Disciples' here: https://bbc.in/3NUh6Ow or wherever you get your BBC podcasts.

03/01/2024

Kupatula kugulira ndi kulipilira ntchito ina ya ndalama ndi chani?

Good morning students๐Ÿคฃ

03/01/2024

To those that have watched the movie, 'SCHOOL DAYS' ๐ŸŽฌ
What's your comment ?

 Anthu lero nkhani ili mkamwa-mkwamwa ndiya Phwedo.Phwedo ndi dzina ndithu, koma osati lenileni. Ili ndi dzina la m'modz...
03/01/2024


Anthu lero nkhani ili mkamwa-mkwamwa ndiya Phwedo.

Phwedo ndi dzina ndithu, koma osati lenileni. Ili ndi dzina la m'modzi mwa anthu omwe ali mufilimu ya School Days, yomwe inatuluka pakanthawi ndithu chaka chatha, koma anthu apatsidwa mpata oyiwonera mosavuta pa You Tube masiku atatu apitawo.

Tumpe Mtaya ndiye adali Phwedo mu filimuyi yomwe ikulongosola nkhanza zomwe ophunzira amachitirana pasukulu zogonera komweko.

Phwedoyo, adali ozunguza komanso wachamba ndi mowa mufilimumo. Kapatula apo, maonekedwe ake adali owopseza komanso auchigawenga.

Pakutha pamasiku atatu, filimuyi yaoneledwa ka 118 000, zomwe zikusonyeza kuti ndiyachikoka.

(by Innocent Kumchedwa- Lilongwe:01/02/24)

30/12/2023

Ambiri a FCB Nyasa Big Bullets ndi a Man U, kwinaku A Mbulingidwa basi Zatherana!!!!

30/12/2023

Ipondeni Fadah mukuopa ndani?

30/12/2023

Yavuta ndi Area 49 kufuna kupindula kawiri.

30/12/2023

One day you will test HIV positive because of forgiving your cheating partner ๐Ÿ˜‚

25/12/2023

Merry Christmas guys to all of you! Enjoy these days with your families, make it special with your loved ones ๐ŸŽ„โœจ

Special, big hug to those who are alone or those who are experiencing difficult days during holiday season. Itโ€™s tough but keep believing. Sending love. โค๏ธ

Friday yanu ikuyenda bwanji
17/11/2023

Friday yanu ikuyenda bwanji

Address

M18
Lilongwe
265

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Social Vibes-Out posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Social Vibes-Out:

Videos

Share