25/04/2023
KODI M,PINGO UKAPULUMUTSA MUNTHU?
Fuso ngati ili ambili amadzifusa ,mwachomcho ,koma malingana ndi chinyengo chomwe Satana adachita kudziko lapasi ,zili zovuta kumanena k*ti m,pingo ukapulumutsa munthu ,
Chiv 12:12, tsoka litalengezedwa lobwela kudziko lapasi ,kamba kak*tsika kwa Lusifala ,dziko linawonongeka ndi kusandulika malo omenyela nkhondo pakati pa chabwino ndi choyipa,
Mulungu adayika mpingo wake umodzi padziko lapasi ,atawuchotsa kumwamba ,kudzela mwa adamu ndi hava, chilichose choyeneleza adawupatsa m,pingowu ,,udapatsidwaso lamulo, koma posakhalitsa panabadwa kupembedza kuwili ,chifukwa cha Satana ,atalowa mwa kaini,Genesis 4:4-8 ,uku kunali kubadwa kwa mbewu ya chinjoka ,yomati chipembedzo ,munthu atha kuchipanga momwe angafunile ,, posalamulidwa ndi Mulungu ayi,
Kuchokela p***a kugawanika kunafalikila , kudziko ,ndizomwe lelo zikuwoneka zokayikitsa k*ti mpingo sungapulumutse munthu , koma tilingalileko izi ,chipulumutso chidabwela ndi Yesu ,kusonyeza k*ti tipite kwa iye ,kodi Mulungu Ali ndi mpingo kudziko kuno? Nanga ntchito yake ndiyachiyani ,mpingowo kudziko kuno?
Yankho mateyu 28:18-20, kuphuzitsa , fuso ngati m,pingo uphuzitsa zosalingana ndi Baibulo anthu mk*tsata zimenezo ,kodi anthuwo akapulumuka? Kodi ngati mpingowo ukuphuzitsa zose zolingana ndi Baibulo anthu mk*tsatila kodi anthuwo akapulumuka?
Mafuso awa ndukhulupilila aliyese wapeza yankho , m,pingo ukumuthandizila Yesu kupulumutsa munthu ,ngati m,pingowo ukuphuzitsa malingana ndi kwa lembedwa ,koma zachisoni lelo anthu ambili ak*ti ndi aMulungu ,ndi aYesu ,koma ,kumeta m,mbali kuli pakati pawo, kuvala zothina, masiketi ong,amba ,
Kupemta milomo, kupemta Zara ,kuvala maliboni,kuvala ndolo, kuvala meshi, kuvala mosemphanitsa ,azimayi kumakhala azisembe,otumikila kumalo opatulika,zosezi Mulungu akukana ,koma mkumati ndife m,pingo waMulungu ,kodi chiphuzitso ichi anthu apulumuka?
Yesaya 29:13-14, Mateyu 15:7-9, Yesaya 9:16, Yesaya 3:12, usapusitsidwe ndi mawonekedwe m,bale sankha Ame