Violence Academy FM

Violence Academy FM Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Violence Academy FM, Box 6678, Lilongwe.

Welcome to �*Violence Acadamy�

This is online Radio station
Yomwe timakhala tikupanga ma interview ma artist osiyana siyana
Ma big artist komaso ma upcoming artists��

22/07/2024

Driemo kupanga zibwana atisiya ngati pop young soon😂

uthenga ndumenewu
02/01/2024

uthenga ndumenewu

Spy-Kay 98
10/10/2023

Spy-Kay 98

Nthawi nka kape

06/10/2023

Osamada nkhawa muli okuda kale

05/10/2023

Kell Kay

Tiyeni uku gyz..
Tikadumphe

01/10/2023

BASI PACHIYAMBI MULUNGU ADALENGA INUYO

13/08/2023

UBWINO KU MWAMBA ALIYESE AKAKHALA NTUNDU WAKE WENI WENI 😯😯😯

01/06/2023

Kunali Gaffah pano Ali kuti?
Kunali 2kings Mhsrip
Kunali Gray matter pano Ali kuti?
Kunali kandapako empire pano akungogulisa chimanga cha anthu ku madimbaku
Kunali lay one pano Ali ku jowen plan alibe
Kunali G paper pano Ali mu lilongwemu ndi dzamba kwa azising'anga aponye comment wa

Kunali ice kid pano nde ndi uyu amavala zofila amagulisa samusa ku Airtel komaso ati ndi ujen.

Kunali Spy k pano nde ulovi wamudyatu ku lifuu ko

Kunali Sheri b awawa nde sankatha kuimba

Kunali Mr love pano anapenga atakhala dzaka zambili asakutchuka

Kunali Tiyo uyuyu nde khalidwe la ice kid lijatu basi

Dear upcoming artists anthu onsewa alembedwawa anatha

Mashasha ndinuyo mukumveka panonu

Nyimbo zomwe amati anayimba bwinozo ndi zomwe zomwezo
Za 2014 zija

Ma producer nonse mupite kwa olusa akakupaseni ma tutorials
Zikomo

30/05/2023

ICE KID ATENGELA KAY-DO MAFIA KU BWALO LA MILANDU

Precious chirwa yemwe amadziwika ndi dzina loti ice kid lero watengera oyimba wina wa chamba cha dancehall mu Boma la salima otchuka ndi dzina loti Kay do mafia ku bwalo la milandu mu Boma lomwero la salima.

Ma report omwe angotipeza kumene akuti ice kid masana a tsiku la chisano anapita pa tsamba la mchedzo(Facebook) nkuyamba kumunyoza Kay do mafia kuti si kadaulo kunkhani ya mayimbidwe,poonjezela Apo ice kid analembaso mawu ena onyoza oyimba winaso odziwika ndi dzina loti Mo B Malawi.

Ice kid ataona kuti sanawayankhulire bwino oyimba anzakewa iyeyu anabwelaso pa tsamba la tchezo lomwero napepesa koma motsindikabe kuti katswili oyimba chamba cha chambayu(Kay do mafia) sathabe kuimba ndipo aphudzile,

Mu mawu ake iye anatamanda oyimba ena amu Boma lomweri kuti ndi anamandwa ku nkhani ya maimbidwe,.

Izi sizinasangalase oyimba wa chamba cha chambayu (Kay do) ndipo iye posonyeza nkwiyo wake anabwelaso poyela kuzaulura za mchitidwe wa kathyali oyimba nyimbo zodikulazi ice kid kuti ndi mgotchana(anyamata ochita mchitidwe ogonana okha okha) zomwe zinaphyesa ntima ice kid kuti afike pomutengera kay do mafia ku BWALO la milandu la salima magistrate court.

Tikudikila chigamuro kuchokera ku bwalo laza milandu

Munali ndi ine muulusi wanu Nkaladi

29/03/2023

Komano wats fridge in chichewa?

27/03/2023

Tiyambe ndi captain wonder by Waxy Kay ili bwanji?

27/03/2023

We are back

Address

Box 6678
Lilongwe

Telephone

+265995370404

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Violence Academy FM posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Violence Academy FM:

Share