Fewaz

Fewaz Never say never until it's over No musicians beat us

Safusa anadya phula uja ndi uyu😂😂😂
03/06/2024

Safusa anadya phula uja ndi uyu😂😂😂

Chizmo Njuchi  koma vamva Izi  zoti wina waziombela Ku chigumula mgalimoto?
25/05/2024

Chizmo Njuchi koma vamva Izi zoti wina waziombela Ku chigumula mgalimoto?

24/05/2024

To all our followers don't get surprised,We are rebranding the name for the sake of our next projects,Stay cool and enjoy.

If you know you know
03/02/2024

If you know you know

New Cookie straight from Kitchen
19/07/2022

New Cookie straight from Kitchen

31/05/2022
23/04/2022

Iyi nde Ichema man

19/04/2022

Tikubwela Kwanu

08/04/2022

MUSAZATINAMIZESO LYRICS
Hook
Musazabweleso Sindingazamveso
Mabodza akowo
Musazafike pakhomo panga
Musazapondeso(Hook ×4

V1.
Nangomva achimwene week yamawa ndikubwela//Zonse umafuna zina ndikugulira ndikamabwela//Ine chimwemwe kusekelera// Diso kunjila ndilandila braz ikubwela//kukonzekela kupha nkhuku braz yayandikila//Kugula mafuta kukazingila//Braz ikafika itibwezela
V2
Anakulonjeza chitenje//umankonda koma iye ngochulikidwa times //Ngati galimoto zakwamanje//Amazimva kutentha ati ali hoti ngati ku nsanje//Ndi bangula ngati Grace ndiulura//Ndimaponda ponda ndimaona mponela//Akazi oyela ndi zodzola//Akugulilidwa magalimo a corrola//
Mpaka kundilora akuesa akolora//Nangomunamiza nde akulira

BUY US THIS NEW TRACKCall or Whatsapp 0881492269
05/04/2022

BUY US THIS NEW TRACK
Call or Whatsapp 0881492269

Address

Dedza

Telephone

+265881492269

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Fewaz posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Videos

Share