Amazing Art Network

Amazing Art Network Graphic Designing| Creative Writing| Inspirations| Talent That Transforms Lives Amazing Art Network, Always Amazing
(15)

-Connected through Art to inspire, motivate and entertain.
-We are a home of creativity.

15/12/2024

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Anzaku Ovey, Hopkin Waho

10/11/2024

Dear child of God, remember He has entrusted you with responsibilities and mandates to fulfill. Though outcomes may seem threatening or scary, draw strength from Christ's example (Hebrews 12:2). He knew His assignment's outcome yet faithfully followed God's instructions.

Philippians 1:6 assures us, "He who began a good work in you will carry it on to completion." Fear not, for God is with you.
As a man or Child of God; do not fear the outcome, follow the instruction.

(Isaiah 41:10, Matthew 28:20).

When you listen to motivational speakers a lot😂
31/10/2024

When you listen to motivational speakers a lot😂

10/10/2024

If you try to fail and succeed, what did you just do?

Goodmorning

A Turkish Airlines flight traveling from Seattle to Istanbul was forced to make an emergency landing in New York after o...
10/10/2024

A Turkish Airlines flight traveling from Seattle to Istanbul was forced to make an emergency landing in New York after one of the pilots collapsed mid-flight, the airline confirmed on Wednesday.

HomeWORLD NEWS Pilot Dies Flying Plane from US to Turkey, Flight Forced to Land Amazing Art Network October 09, 2024 0 A Turkish Airlines flight traveling from Seattle to Istanbul was forced to make an emergency landing in New York after one of the pilots collapsed mid-flight, the airline confirmed....

07/10/2024

Why does your nose run and your feet smell?

In life, we often encounter moments where decisions feel overwhelming. Whether it’s a career move, a personal relationsh...
07/10/2024

In life, we often encounter moments where decisions feel overwhelming. Whether it’s a career move, a personal relationship, or a financial investment, the weight of making the "right" choice can be paralyzing. Yet, there’s an age-old piece of wisdom that often goes unnoticed: "If you cannot decide, the answer is no." This seemingly simple statement carries profound significance, reminding us that indecision, in many cases, is a decision in itself. But why is "no" the answer when clarity evades us?

HomeOPINION Why "No" is the Right Answer When You Can't Decide Amazing Art Network October 06, 2024 0 In life, we often encounter moments where decisions feel overwhelming. Whether it’s a career move, a personal relationship, or a financial investment, the weight of making the "right" choice can b...

Much has been said about Generation Z and their supposed aversion to reading. In an era dominated by social media, many ...
07/10/2024

Much has been said about Generation Z and their supposed aversion to reading. In an era dominated by social media, many assume that young people have abandoned books in favor of quick, digital content. However, the reality is far more complex

HomeOPINION It’s Not Just Gen Z Who Don’t Read Redson Kandozi October 01, 2024 0 Much has been said about Generation Z and their supposed aversion to reading. In an era dominated by social media, many assume that young people have abandoned books in favor of quick, digital content. However, the ...

Have you checked our blog yet?Check it out by clicking this link
07/10/2024

Have you checked our blog yet?
Check it out by clicking this link

Unlocking Malawi's Film Potential Amazing Art Network October 06, 2024 By REDSON KANDOZI & CLARA WADI Malawi's movie industry has demonstrated significant growth …

👏👏👏❤️❤️
05/10/2024

👏👏👏❤️❤️

We are in today's paper!!!
Sharp sharp Crisps

In a significant legal development, South Africa’s Constitutional Court announced it will, next month, review a petition...
04/10/2024

In a significant legal development, South Africa’s Constitutional Court announced it will, next month, review a petition from two opposition parties seeking to revive impeachment proceedings against President Cyril Ramaphosa. The petition centers around a scandal involving over $500,000 in cash, which was allegedly hidden in a sofa at his Phala Phala ranch and later stolen.

HomeWORLD NEWS Court to Revisit Ramaphosa Impeachment Case Amazing Art Network October 04, 2024 0 In a significant legal development, South Africa’s Constitutional Court announced it will, next month, review a petition from two opposition parties seeking to revive impeachment proceedings against P...

"Achimwene mukwatire" sindikudziwa kuti mungawamve bwanji mawuwo maka atalankhulidwa ndi munthu yemwe ndi m'chemwali wan...
04/10/2024

"Achimwene mukwatire" sindikudziwa kuti mungawamve bwanji mawuwo maka atalankhulidwa ndi munthu yemwe ndi m'chemwali wanu yemwenso ndi otsiriza pakubadwa. Ineyo mawuwo adandidzizimutsa. Nthawi imeneyi nkuti nditapita kumudzi kwathu ku Mwanza.
You can read more by simply following this link »

HomeFICTION MY CHRISTINA CHAPTER 6: BWATO LA MISOMALI Amazing Art Network September 29, 2024 0 "Achimwene mukwatire" sindikudziwa kuti mungawamve bwanji mawuwo maka atalankhulidwa ndi munthu yemwe ndi m'chemwali wanu yemwenso ndi otsiriza pakubadwa. Ineyo mawuwo adandidzizimutsa. Nthawi imeneyi nkut...

MY CHRISTINA CHAPTER 5 Chipinda chandendecho chinali ngati gahena, malingaliro anga anali atasochera m'chizunzo cha chiz...
04/10/2024

MY CHRISTINA
CHAPTER 5

Chipinda chandendecho chinali ngati gahena, malingaliro anga anali atasochera m'chizunzo cha chizunzo, chomwe chinkapangitsa kuti ndisowe tulo lomwe ndinkalifunitsitsa.
Dziko lidali likunong'oneza zinsinsi zoyipa m'makutu mwanga, zinsinsi zomwe ngati sudafike kumaloku sungazidziwe. Ndinene mosabisa kuti mkati mwandendeyi mudali mukuoneka nkhope zaukapolo zomwe zimkavumbulutsa zinsinsi za m'mene miyoyo yamkatimu imazunzikira.

M'makoma andendeyi mudali mutalembedwa mawu omwe kuwanena pano mungathe kuona ngati abale anu omwe ali malowa sadzabwerako amoyo. "Kunsabwera" khoma lina lidali litalembedwa choncho ndipo zidapangitsa malingaliro anga kuyamba kufanana ndi wamisala maka ndizomwe ndinkaganiza munthawiyo.

Manong'onong'o a chikayiko anadutsa mbali ina ya malingaliro anga kwinaku malirime awo ankhanza akuluka nthano za chipsinjo komanso chisoni chomwe chinkaoneka pankhope za ambiri ndidawapeza kumaloku.
"Uzolowera, nane ndinkatero" ndidamumva wina akundirankhula dere ndipo ndidapukusa mutu.
Ndikadazolowera bwanji chonsecho chomwe ndidalakwa nkuti ndisakuchidziwa bwinobwino? Ndikadakhala ndidali olakwa ndithu mbamba ndikadatha kumvetsa kuti kudali koyenera kulandira chiweruzochi.

Zokumbukira zam'malingaliro anga zomwe zidali zogawanika komanso zopotoka, zidandinyoza ndi kuseka moyo womwe ndidali pafupi kuwutaya komanso ndi ufulu womwe udachotsedwa. Ndili mkati mwa malingaliro anga, mantha adatenga mawonekedwe owopsa omwe ankapangitsa kuti ndipanikizike mkatimu.
Kusungulumwa kunafika penipeni, panthawiyi ndimkamuganizira Christina. Adali bwanji? Ankaganizirabe za ine? Bwanji m'masiku amenewa sadabwere kuzandiona? Adali nanedi m'chikondi? Mafunso onsewa nkuti akupikisana kuti ayankhidwe koma adalibe yankho lililonse.

Maloto ndi zikhumbo zomwe poyamba zinali zamoyo ndizolimba, tsopano zinali zosweka ngati kalirole. Munthawiyi ndinkakumbukira zambiri zomwe tinkanong'onezana ndi Christina, kumusowa kwanga kudapangitsa kuti ndiziyiona nkhope yake ndipo ndichokhacho chinkapangitsa kuti maganizo anga akhale osabalalika mkati mwandendeyi.
Tsiku lililonse linali nkhondo, kulimbana ndi mafunde akutaya kwa mtima amene akanatha kundiwononga. Sinanga yemwe ankapangitsa moyo wanga kukoma m'masiku amenewa adali asakuonekanso kumaloku?

Akaidi enawo ankangondiyang’ana ngati kuti ndine mzukwa, mzukwa womwe ukuvutitsa m’malo abwinja a moyo wawo.
Ena mwa iwo maso awo adali owumitsidwa ndi zowawa zomwe ankadutsamo kapenanso kuuma mtima komwe kudali mkati mwawo. Inde, adalibe nkhope zachisoni ndipo nkhope zina zidali m'katimu zinkafotokoza za milandu yomwe adapalamula.

Ndidaona kuti uyu adali ganyu wankulu. Kuganizira zamaonekedwe awowa kudali kotayitsa nthawi ndipo m'malo moika mtima wanga pandende ya Chichiri-yi ndidaika mtima wanga mundende yakumusowa Christina. Ndinkazifunsa kuti panthawiyi ankatani ndipo ndichani ankaganiza. Sizidali zopindulitsa kwenikweni koma zimandithandiza kuti usiku watsiku limeneri usatalike. Apatu nkuti nditangotha masiku awiri ndili pandendeyi koma nkhani yanga isadapite ku bwalo la milandu.

Nditapita ku polisi kuja ndidazindikira kuti Elias adali m'modzi mwa iwo. Iyeyu adali wapolisi wachinsinsi ndipo zonsezi ndidadziwira patsikuli. Kupolisiku mkuti nditakanika kufotokoza momwe ndalama komanso mapepala ena okhudzana ndikagwiritsidwe ntchito kachuma kaku kampani yomwe ndinkagwira ntchito adapezekera muchikwama changa.

Ndinkalephera kumvetsa kuti ndindani yemwe adaika zinthuzo mu chikwamacho koma mutu wanga tsopano nkuti utaima pachiganizo choti adali Elias yemwe adachita zimenezi. Kwa zaka ziwiri zomwe tidadziwana zinkaoneka kuti adali atandibisira chinthu chimodzi chomwe chidali chofunika. Inde malo ake antchito.
Ndidayamba kukumbuka zatsiku lomwe tidali titapitira limodzi kumalo omwera mowa kuja. Mkutheka iyeyu adaika zinthuzo ineyo nditachokapo? Ndidazifunsa funsolo koma sindinkatha kukumbukira kwenikweni. Usiku umenewu tulo lidavuta kubwera ndipo ndidachezera kuganiza za tsiku lotsatiralo poti ndilomwe mlandu wanga unkayenera ukalowe ku khoti.

M'mawa wa tsikulo utafika chisokonezo chachikulu nkuti chitandipeza ndipo ndimasowa mtendere mumtima. Makolo anga ndidali ndisadawauze kalikonse ndipo sindinkafuna nditero komano kufika nthawi yomwe ndinkayenera ndipite ku bwalo la milandulo mtima wanga udayamba kugunda ndi mantha pozindikira kuti munyengoyi ndidali ndekhandekha. Ndisadanyamuke kundendeku ndidalandira uthenga oti munthu wina ankandifuna ndipo chiyembekezo changa ndimkayesa adali Christina koma adali bambo yemwe sindinkamudziwa.
"Wandituma Christina. Ndikhala okuimilira pamulandu umenewu" adafotokoza chomwechi bamboyo yemwe adali wachikulire ndithu.
"Iyeyo ali kutiko?" Ndidafunsa. Kusapezeka kwake sikuti kunkangondipanga kukhala osungulumwa kokha, koma kunkandipanganso kukhala wamantha.
"Akulongosola zinthu zina kuti tik**apita kukhoti tikhale chikwanekwane"
"Zinthu zake chani?" Ndidafunsa mosawonetsa kusawakhulupirira kwanga.
"Akhala mboni yako, komanso payekha ali ndi umboni omwe utha kutsutsa zonsezi" adatero uku akutulutsa kabuku kake kuti azilembapo. Ndidaona kuti ankaziphweketsa zinthuzi. Sindikudziwa chifukwa chiyani ankatero koma kusankha kukhala ondiyimirira ndidaona kuti ankazitayitsa nthawi.
Yemwe adandikonzera mulandu umenewu adali ndi chiwembu chachikulu ndi ine ndiye tsogolo lachipambano ndinkaliona lochepa zedi.
"Alipo yemwe ukumukaikira kuti akukuchitira chiwembu pankhani imeneyi?" Ndidafunsidwa funsolo bamboyo.
"Sindikudziwa choti ndiganize choposera kukana mulanduwu. Ngati Christina angapezedi umboni ndiye kuti pakutha kwatsiku lalero ndituluka. Zimenezo ndizomwe ndikuganiza" ndidayankha ndipo bamboyo yemwe sindidafune kudziwa dzina lake adanyamuka kumapita.

Mulandu wanga unkayenera uyambe chakumasana atsikuli moti nthawi itakwana ndidatengedwa kuti ndikaonekere kubwalo lamilandulo.

Kufika kubwaloli pamasana atsikuli sindidakhulupirire zimene maso anga ankaona. Christina adali ali limodzi ndi makolo anga komanso m'chemwali wanga ndi m'ngono wanga uja. Ndidali ndimafunso ambiri koma panthawiyi sindikadatha kufunsa mafunsowo.
Mosataya nthawi ndidalowetsedwa m'bwalo la milandulo ndipo tsopano ndimazimva ngati ndidali mung'anjo yamoto. Ndidayang'ana mbali yomwe kudali mayi anga. Maso awo nkuti akunena zamisozi yomwe inkakanizidwa kuti ituluke ndipo ndidadziwa kuti chachikulu ankayembekeza kudali kuona mwana wawo akumasulidwa unyolo ndikutchulidwa mfulu.

Posakhalitsa oweruza adayamba kulankhula. Adali ndinkhope yomwe ndikadaifotokoza ndiri m'bwalo lamilandulo ndithu akadatha kunditsekulitsira mulandu wina koma ndidaipirira ngakhale idali yowopsa.
"Tikupempha wodandaula kuti atiuze tili muno madando awo. Koma musayambe, mudayenera kugwira baibulo ndikumbira pamaso pagulu lino kuti chirichonse chomwe munganene ndichoona" adatero m'modzi mwa oweruzawo ndipo ndidaona bwana anga akulumbira.
"Ndinthawi yanu omwe mukuimirira mbali yonse yodandaula" adalankhula oweruzayu.
"Olemekekeza, mudali mu mwezi wa January chaka chatha pomwe tidaona kuti kunthambi yathu yosunga ndikuyendetsa chuma zinthu sizimayenda bwino. Ndikati sizimayenda bwino ndikutanthauza kuti kunkabedwa ndalama koma nthambiyi inkayesetsa kuonetsa ngati chilichonse chidali m'chimake" adafotokoza dere oyimirira kampani yomwe ndinkagwirako ntchitoyi ndipo ndidayamba kuona kuchedwa kuti nthawi yanga yolankhula ifike.
"Munzeru zathu tidaganiza zopeza anthu ofufuza omwe ataona m'mene chuma chathu chinkayendera, adaona kuti bambo Malumbo Jalasi adali akuononga chuma cha kampani yathu. M'menemo mudali m'mwezi wa August kumayambililo" adapitiriza kufotokoza dere oyimirira kampani-yo ndipo ndidaona bambo ankandiyimirira pamulandu uja akudzambatuka.
"Kodi tabwera kuzakamba nkhani yake iti? Yakupezeka kwa ndalama zomwe zikuganiziridwa kuti zinabedwa ndi bambo Malumbo kapena yakusokonekera kwa chuma ku kampani yanu kuyambira chaka chatha?" Adafunsa dere bamboyo ndipo funso lakero lidapangitsa kuti oweruza ayambe awuza yemwe ankaimirira kampaniyi kuti anene tchutchutchu wachimene adasuma kubwaloli.
Kubwera kwa funsolo kudapangitsa odandaulayo kukamba zokhudzana ndikupezeka kwa ndalama zija ndimapepala aja muchikwama changa ndipo tsopano idakwana nthawi yoti nane ndiyankhepo pazomwe oyimira kampaniyi ankafotokoza.
"Bambo, mulandu omwe inu mukuimbidwa ndiokhudza kubedwa kwa ndalama komanso mapepala ena okhudzana ndichuma akumalo anu antchito akale kutsatira kuchotsedwa kwanu. Mukuwukana kapena mukuwuvomera?" Adafunsa dere oweruzayo.
"Olemekekeza, ndikuwukana" ndidatero maso anga ndikuwathawitsa pankhope yake. Ndikuti amaopsa.
"Tamva zimene odandaula adali nazo. Mbali yanu muli ndimafunso aliwonse oti mufunse odandaulawa pachilichonse chomwe awuza bwalo lino?" Adafunsa dere ndipo ndidaona ondiyimirira wanga akuima kuti afunseko mafunso ake.
"Olemekekeza, ndichifukwa chiyani pakufotokoza kwanu kwankhaniyi pachiyambi mudafuna mukambe zakusowa kwandalama komwe kudachitika kuyambira chaka chatha? Nthawi yonseyi bwanji simudafune kuwasumira bambo Malumbo ngati mudali ndi umboni onse? Bwanji simudawayimitse pantchito kutsatira kuona zimenezi? Nkolakwa kunena kuti mwakhala mukuwasungira bambowa chiwembu? Nkulakwa kunena kuti mudangofuna mupezelepo omunamizira nkhani yonseyi kutsatira kuchotsedwa kwawo kwantchito? Titha kukhala olakwa kunena kuti zinthu zomwe zidapezeka m'chikwama mwawo mudachita chowaikira kuti mupeze omunamizira? Mundilole ndiyime p***a" Adaphaphalitsa mafunsowa bamboyu ndipo m'bwaloli mudali chete kumvetsera.
Oyimira kampaniyi adakana mwa mafunso adafunsidwawo pofotokoza kuti adali ndi umboni omwe unkatsimikizira zonsezi.
Tsopano mwayi udali utaperekedwa kumbali yathu kuti ndifotokoze zomwe zidachitika komanso kuikapo umboni omwe ukadatsutsa zonsezi.
Sindidakhulupirire zimene ndidaona maka pa umboni omwe udabwera ndi Christina.
Iyeyu nkuti atapita ku malo omwera mowa omwe tidapitako ndi Elias ndipo adapempha ngati kudali kotheka kuti awone zimene zidajambulidwa pamalowa kutengera kuti padali ma camera.
Pamenepo ndipomwe adaona Elias akutenga ndalama zija ndimapepalawo nkuika muchikwama changa panthawi yomwe ndidapita kokataya madzi.
Chifukwa chobalalika chikwama chija sindidachigwire m'masiku amenewo koma chifukwa ndidali nditamuwuza Christina m'mene ndidayendera tsiku limenero, adakwanitsa kusaka umboniwu mongoganizira chabe m'mene mapepalawo adapezekera muchikwama muja.
Tsopano nkhani yonseyi idatembenuka ndipo zinkaoneka kuti anthuwa adali nane chiwembu.
Koma chifukwa chani? N'chifukwa chani Elias ankakhudzidwapo? Kapena adali atapezerapo mwayi chabe poti ndidali nditachotsedwa ntchito? Mafunsowa nkuti akuyenda m'mutu mwanga ndipo panthawi yomwe ndinkabwerera kunyumba kwanga ndidazunzika nawo.
Zinthu zidali zitachoka kwa ine ndipo zidasamukira kwa Elias yemwe sindinkadziwa kuti zimuthera bwanji. Ndidayamba ndazitaya ndipo ndimkamuyang'ana Christina yemwe ankatiyendetsa pagalimoto lake.

KUSAKA MKAZI WA BANJA-MIRABELOLEMBA: YAMIKANI KUMZINDANDIME YACHIKHUMI NDI CHISANU NDI CHITATUMalo okhawo amene tikanaka...
03/10/2024

KUSAKA MKAZI WA BANJA-MIRABEL

OLEMBA: YAMIKANI KUMZINDA

NDIME YACHIKHUMI NDI CHISANU NDI CHITATU

Malo okhawo amene tikanakamupeza katemera ndi m’dziko la South Africa, mak**aka kuchipatala chimene wodwalayo amasungidwako. Poti Eva anali atakonzeka kumangotsala kumuwuza Mirabel kuti ndakonza zochoka naye mdziko muno m’dima ukangoyamba. Koma sindimapeza njira yabwino yomuwuzira kuti asavute kuvomereza. Kupatula yoyambitsaso nkhani ya mgwirizano wokhala ndi mwana ija.

“Ungazikonde bwanji titakapangira mwana wathu woyamba muchipinda chapamwamba ku hotel inayake m’dziko la South Africa?” Ndinamufunsa.
“Ukutanthawuza tichite kuchoka kuno mpaka South cholinga choti ndikangotenga pathupi nkumabwerako basi? Imeneyiso yayambira pati?” Anandiyang’ana mosakhulupirira.
“Bwanji ukudabwa siiwe namwali?”

“Oh, ukufuna ulendo wanga woyamba ukakhale wapadera, ndiwe wachikondi komanso wanzeru. Zindipangadi kuzimva kulemekezedwa ndiye palibe vuto ndavomera.” Anatero akundikumbatira mkono wamanzere.
“Mukudziwa kuti ndikupanda ulemu komanso kulakwa kumayankhulana zimenezi kenako ndikumakumbatirana munthu wina alipomwepo sichoncho? Simukundilemekezatu pamenepa mukudziwa?” Anatero Eva kudandaula akudzuka nkumalunjika kuchipinda chophikira.
Anapita kukangotenga madzi okumwa odzidzira.

Atabwerera anazamuwuza Mirabel chilungamo kuti cholinga chachikulu chomwe timakonzera zopita ku South Africa sichinali kugonana. Koma kuti tikafike kuchipatala chimene wakhala akusungidwako kukamusakira mankhwala kapena katemera wamtundu omwe ukufunikawo ndikukamubaya kuti asamadwaledwale ngati kale.
Sindinakondwe kuti chilungamocho chiwululidwe motero chifukwa ndimadziwa mwini ulendo sagwirizana nazo. Ndiye pofunabe kuti pasakhale kukangana ndinamulonjeza tikakafika mdziko lachilendolo choyamba tikakwaniritsa kaye mgwirizano wathu. Zimenezo ndizonse zomwe ndimaganiza kuti Mira afuna kumva panthawiyo. Kuti kutsaleno kucheza wamba podikira dzuwa lipendeke nthawi yaulendo ifike. Koma mkazi wokondedwa anafuna kuwugwiritsa ntchito mpata umenewo kuti adziwe zinthu zomwe sindinamuwululire nthawi yonseyi.

Anafunsa zaukulu wa kampani yanga ndi zomwe imapanga, mafunso amene ankafunitsitsa nditamuyankha tili ku Mayani. Mosiyana ndinthawi imeneyo tsopano ndinali wokonzeka kumuyankha, koma sindinamuyankhe. Ndinamuwuza mbali yokhudza umoyo wanga wantchito yomwe akanakonda kuidziwa siyokhudza kampani yazochitika zosiyanasiyana yomwe ndilinayo. M’malomwake amangofunika kudziwa kuti ndine Loya, ndipo ndikuyambitsa kampani ya maloya oti ndizithandizana nawo kupezera chilungamo anthu omwe amaponderezedwa m’njira zosiyanasiyana.
Ndinamuwuza chimenecho ndichifukwa chomwe ndasankhira kumuthandiza Carol. Chifukwa chomwe ndidasankhira kumuthandiza Eva, komanso chomwe ndikuganizira kuti tikakafika m’dziko la South Africa ndikadziwa bwino phata la nkhani yake. Nditayankhula zimenezo anandiyang’ana mokhumudwa pozimva kuti wataya nthawi yochuluka akumafotokoza zinthu molambalala.

Zimene ankaganiza zokhudza moyo wanga wantchito zinali kutali ndizomwe ndidamuwuzazo. Ndiye mwina zinthu zina sankandiwuza poganiza kuti sindikanazimvetsa. Tsopano amangofunadi kudziwa zokhudza mbali yothandiza anthu kulimbana ndi milandu yoponderezedwa yokhayo. Koma samafuna kudziwa nthawi yomweyo, chifukwa anachoka kaye monyanyala kupita kuchipinda kumakalira. Nditamutsatira anandiwuza ndimupatse mpata wokhala yekha. Anali atandikwiyira podzimva kuti ndikanamuwuza pachiyambi bwezi akukhala wopanda nkhawa.
Zifukwa zamkwiyo wakewo zinali zomveka ndiye ndinamusiyira mpata womwe amafuna pobwelera kuchipinda chochezera kuti ndizikatayitsa nthawi pocheza ndi Eva. Chomwe sindimadziwa nchoti naye dotoloyo anali nane milandu yogonera, chifukwa atangondiwona ndikubwerera ndekha anaseka monyodola.

“Bwanji?” Ndinamufunsa ndikukhala.
“Kufatsa konse munkachita kusukulu kuja kani munkalingaliraso zozakhala ndi mkazi. Koma ameneyo athandiza?”
“Palivuto penapake?”
“Lilipo koma iweyo sungaliwone. Ukudziwa kuti kusukulu kuja atsikana ambiri tinkakufuna?” Anandiyang’ana m’maso.
“Palibe adandiwuza kuti ankandifuna koma ndinkadziwa kuthekera kunalipo koti winawake kapena angapo ankandifuna.”
“Nde munkangosankha kukhala odzikonda chonchija?” Anafunsaso.
“Kutanthauza kuti chani?”

“Kutanthawuza kuti anthu osalakwa ngati ineyo ndiyamba kumwa ma ARV chifukwa chakudzikonda kwakoko. Ndichani chomwe enafe tidalibe chomwe mwachipeza mwa wodwalayi? Amuna ena sadzadziwadi chomwe azakapsere.” Anatero nkudzukapo kumaloweraso kuchipinda chophikira koma ulendo uno monyanyala atayamba kulira.

Kuyankhula kumeneko kumatanthauza kuti alinane nkhani ndipo siinali yovuta kuiganizira. Koma chifukwa choti kuipa kowapatsa akazi mpata oti asokoneze mutu ndimakudziwa bwino sindinalore ndimuphwekere. Ndimayeneraso kudzipatsa mpata woganiza modekha, ndiye ndinakhala pabalaza pomwepo mpaka tulo linandipeza.
Nditangotseka maso sindinadziwe kuchuluka kwa nthawi yomwe inadutsa kuti ndiyambe kulota. Koma mwachangu momwe zimachitikira ndinadziwona ndili muchipinda chotseka ndikuvula zovala zaukwati.

‘’’’Munali m’chipinda chosiyana ndichanga zomwe zidandizindikiritsa kuti sindili kunyumba, koma mu hotel. Ndinali m’menemo patsogolo pa k**a wokongoletsedwa bwino ndikuchotsa chovala chimodzichimodzi mpaka ndinatsala ndi kabudula wamkati. Chilichose chimachitika mowonetsa kuti ndimadziwa chomwe ndimachita.

Kuchokera pamenepo ndinayenda ndinsangala zosefuka kulunjika kukachipinda kosambira komwe kumamveka kuthamanga kwa madzi ndi kuyimba kwa mawu anthetemya. Dutswa lililonse la thupi langa limandiwuza kuti mkazi anali kumenekoyo ndi Mirabel, zomwe zidandiwonjezera chimwemwe. Nditafikako analidi Mirabe wachibadwire yemwe adandiyang’ana mokopa akundikodolera pafupi naye. Unali usiku waukwati wathu ndipo timapanga zosambira limodzi. Ndinjala ya zilakolako yomwe imalamulira minyewa yanga mukanthawi kochepa tinali titayamba kupsopsonana. Chilichonse chomwe chimachitika chinali m’malo mwake kufikira pomwe ndidatsekula maso.
Nkhope ya Mirabel amene ndimapsopsonana naye inali momwe ndimamudziwira, koma kumbuyo kwake kunali kutaimaso iyeyo.

Zinali ngati ndili ndi munthu m’modzi “muwiri” zomwe zidapangitsa mtima wanga kugunda mwamantha. Nditapukuta nkhope mofuna kutsimikiza ngati ndimawonetsetsa palibe chomwe chidasintha. ndinali ndidakali ndi akazi awiri onsewo owoneka kuti ndi m’modzi.’
Muchochitika chotsatira mkazi yemwe ndimapsopsonayo atandifunsa kuti tinali titasiya chifukwa chani, wakumbuyo uja anawoneka wokwiya. Iye anakuwa kunena kuti ndimayenera kumapsopsonana ndiiyeyo, kenako anatenga kachidutswa ka kalilore wosweka nkumafuna azibaya.’’’’

Ndinazizimuka, koma modekha popanda kukuwa kuti ndingofikira kumvetsera kusinthana mawu kolimbana pakati pa Mirabel ndi Eva. Sindinakwanise kudziwa kuti amakangana zokhudza chani chifukwa atangozindikira kuti ndadzuka anasiya. Anandiwuza sanafune kundidzutsa ndiye ndimayenera ndikasambe kenako ndidye chifukwa nthawi yomwe ndinawauza kuti tinyamuka inali itawandikira.
Kutengera nthawiyo ndinali nditachedwadi kudzuka zomwe zimatanthawuza kuti ndingathe kukanika kufika malo angapo munthawi yake. Pofuna kuti nthawi iliyonse imene ndinaiyerekeza ik**akwana ndikhale nditafika pamalo amene ndimawaganizira sindikanataya nthawi ndikusamba kapena kudya. Ndiye ndinapita kuchipinda kukangotenga chikwama ndi thenifolo yaing’ono komanso fungulo za galimoto yoti tiyendere.

Aliyense wa akaziwo anali atakonzeka koma mosiyana ndi Eva, Mirabel anafuna kudziwa kaye kuti tiyenda bwanji. Ndisanamuyankhe anandiwuza sakanalora kukhala m’galimoto kuchokera ku Malawi mpaka kum’mwera kwa Africa, zomwe zimandipezetsa vuto langa loyamba.
“Palivuto lanji ndikuyenda pagalimoto?” Ndinamufunsa.
“Mtundawu ndiwautali ndinamva kuti anthu akakwera bus pomakafika kumeneko miyendo imakhala itatupa ndiye ine ayi.”
“Kutanthauza kuti zaka zonse zomachoka ku South Africa kubwera kunoko nkumabwelerakoso sunayambepo utayenda pagalimoto?” Anafunsa Eva.
“Ukufuna kudziwa kuti ndili ndichuma chochuluka motani ulinayo nthawi yokwanira kumvetsera?” Anayankhana.

Patadutsa kanthawi akuyang’anana modelerana ndinamuwuza Mirabel ndilibe ndege yangayanga. Komanso kukanakhala kupanda nzeru kukafika pabwalo lokwerera ndege. Pofika nthawiyo nyumba zonse zowulutsa mawu amphepo ndi kanema zinali zikulengeza uthenga wakubedwa kwake. Ndalama zomwe zingaperekedwe ngati mphotho kwa munthu womupeza kapena wopereka uthenga othandizira kuti apezeke zinali zikuwonjezeredwa ngati mchere mu nsuzi. Zithunzi zake zinali zikumatidwa malo alionse owonekera, ndipo nkhani yake inali imodzi mwazikuluzikulu zomwe zimamanga nthenje m’magulu ochezera pa lamya.
Ndinamuwuza kuyenda pagalimoto inali njira imodzi yokhayo ndipo timafunika kuchita changu.

Ngakhale padalibe ganizo lokwera ndege kuchokera kunyumbako ndinayendetsa galimoto molunjika ku Lumbadzi. Kumeneko ndimayenera kukakumana ndi munthu woyamba oti abweze ngongole. Koma nditangochoka munsewu waukulu kukhotera wakubwalo la ndegeko ndinadabwa kupeza apolisi atatseka nsewu. Kuchokera kwa anthu eni galimoto omwe anali ataimitsidwa ife tisanafike ndinawuzidwa kuti pali malo atatu otsekedwa ndi apolisi, ndipo aliyense wochokera kapena kupita komwe timalowerako akumaimitsidwa. Zimenezo ananena zikuchitika kuti afufuze mtsikana yemwe wabedwa kutengera zigawenga zomwe zamuba zitafuna kutuluka naye mdziko muno.
Nditayang’ana kutalika kwa mzere wa galimoto zoimitsidwazo ndinazuma moyamika. Ndinazimva kulemerera kwamtundu winawake podziwa kuti ndikuyang’anira munthu wofunika kwambiri. Ndipo zimandiwonjezera makani omuthawitsa mpaka ndikafike pa phata la chilichonse chomwe ndikukaikira. Popeza galimoto yanga inali kumbuyo kwenikweni ndinabwerera komwe idaima kuti ndikaitembenuze ndiyesere njira ina. Nditafikapo ndinapezelera mkangano pakati pa akazi omwe ndidasiya mgalimotowo omwe unadula atangondiwona.
Nditawafunsa chomwe chimachitika pakati pawo sindinayankhidwe, m’malomwake nawo anandifunsa chomwe chimachitika panjapo. Naneso sindinawayankhe.

Kuchokera kumeneko njira zomwe tidayenda kupita kumalo ena oti ndikabwenzeredwe ngongole zinaliso ndi malo otchingidwa ndi apolisi moti ndinataya nthawi yochuluka kuwazemba. M’mene ndimakumana ndimunthu yemwe ndimamupitira kumeneko akaziwo anali atadziwa chomwe chimachitika. Kwa Eva funso lomwe linalipo ndiloti Mirabel ndindani. Mak**aka kuti ndiwofunikira kwambiri bwanji kuti apolisi aboma azikhala akugwiritsidwa ntchito choncho mudzina lake. Yakho lomwe sindinamupatse linali loti ndiwolemera kwambiri komanso abale ake ndi akhama lothetsa mankhalu.
Funso linali limenelo kwa Eva, pomwe kumbali ya Mirabel funso lomwe linalipo limabwera chifukwa cha nkhawa. Powona ndimomwe misewu timadutsayo inalili anandifunsa kuti dongosolo langa linali lotani. Amafuna kudziwa kuti tikafika bwanji kudziko lomwe timapitalo chifukwa mwanjira iliyonse zimamuwonekera zosatheka. Zinalidi zosatheka koma osati kwaineyo. Kuti amvetsetse ndinakhosomola kaye kukonzekeretsa kukhosi.
Ndinamuwuza nthawi yomwe ndidali wosauka chinthu china chomwe ndinkawopa chinali kugona ndi njala kapena kuwonedwa ndi nsabwe pagulu. Nditayamba kutolera chuma ndinkazimva kuti ndathana nawo mantha otero, ndipo zinalidi choncho. Koma sikuti ndidali nditathana nazo.

Nzotero poti ndidazindikira kuti mantha omwe munthu wosauka amakhala nawo ak**alemera amakhudza chuma chake. Maka chifukwa cha mawu ena omwe amanena kuti chumacho ndi nchira wakhoswe. Nditayamba kutukuka nane ndinkawopa kuti chinachake chikanatha kuchitika mpaka ndikanasaukaso. Ndiye ndidafuna kumanga moyo wanga ngati chipupa cha nyumba yachigayo, kuti uzakhale wopilira kugwedezedwa kwamphanvu. Ndinapanga zimenezo posiya ngongole zosabwenzeredwa ndi kuwachitira ena zinthu zondipatsa ulemu wokhazikika. Dongosolo lomwe ndinali nalo ndiloyenda njira yonse ndikutolera ngongolezo komanso kulandira ulemu mpaka kum’mwera kwa Africa.
Mkati mwa dziko la Malawi kuthekera kogwidwa kunali kukunkera kukula ik**atha mphindi iliyonse. Titatuluka mzinda wa Lilongwe movutika zochitika zonse zinawonetsa kuti moyo upitiirirabe kuvuta tikayenda mwachindunji. Ndiye m’malo mwanjira zachizolowezi zimene galimoto zopita ku South Africa zimadutsa, ine ndinatulukira m'boma la mchinji. Ndimazimva kuti tiyenda bwinoko tikadutsira m'dziko la Zambia kuti tikasamalidwe ndi mai wotchedwa Tabitha.

PANGANI LIKE, COMMENT KOMASO SHARE.
MUKHOZA KUGULA PDF YA NKHANIYI POLUMIKIZANA NDI MLEMBI 0996683675

Home MIRABEL Unknown October 03, 2024 0 KUSAKA MKAZI WA BANJA-MIRABELOLEMBA: YAMIKANI KUMZINDANDIME YACHIKHUMI NDI CHISANU NDI CHITATUMalo okhawo amene tikanakamupeza katemera ndi m’dziko la South Africa, mak**aka kuchipatala chimene wodwalayo amasungidwako. Poti Eva anali atakonzeka kumangotsala ...

At least 45 people have lost their lives, and 111 remain missing after two migrant boats capsized off the coast of Djibo...
02/10/2024

At least 45 people have lost their lives, and 111 remain missing after two migrant boats capsized off the coast of Djibouti on Tuesday. The boats were carrying migrants returning from Yemen when the tragedy occurred.

HomeWORLD NEWS 45 Dead, Over 100 Missing After Migrant Boats Capsize Off Djibouti Amazing Art Network October 02, 2024 0 At least 45 people have lost their lives, and 111 remain missing after two migrant boats capsized off the coast of Djibouti on Tuesday. The boats were carrying migrants returning....

The battle for the 2024 Super League of Malawi title intensifies as the top three teams—Silver Strikers, Mukuru Wanderer...
02/10/2024

The battle for the 2024 Super League of Malawi title intensifies as the top three teams—Silver Strikers, Mukuru Wanderers, and FCB Nyasa Big Bullets—continue their relentless pursuit of championship glory.In the latest round of matches, Silver Strikers were held to a goalless draw by Bangwe All Stars, maintaining their unbeaten streak since the start of the season.

HomeSPORTS Silver Strikers Lead as Mukuru Wanderers Close Gap in Super League Title Race Amazing Art Network October 02, 2024 0 The battle for the 2024 Super League of Malawi title intensifies as the top three teams; Silver Strikers, Mukuru Wanderers, and FCB Nyasa Big Bullets continue their relentl...

In today’s world, the journey to financial success often seems to be all about having money. It's easy to think that wit...
02/10/2024

In today’s world, the journey to financial success often seems to be all about having money. It's easy to think that without a significant starting capital, you can’t get anywhere in the world of investments or entrepreneurship. Yet, this perception might be more of a mental barrier than a financial one.

There’s a growing belief that the true asset any investor has isn’t money—it’s their mind. This notion pushes back against the conventional wisdom that wealth comes from starting with a full bank account. Instead, it argues that wealth is built from the power of knowledge, strategy, and leveraging resources beyond your own.

Mind Over Money: The Real Investment Starts Here

When you think about investing, the first thought is often about where to find the money. However, successful investors and entrepreneurs often begin without vast sums of capital. They start with something far more valuable—understanding.

At its core, investing with your mind means recognizing opportunities and understanding the principles that drive financial growth. Whether it’s through understanding market trends, grasping the mechanics of a business sector, or knowing how to create strategic partnerships, the power lies in what you know. Mastery of knowledge and how to apply it is what separates those who thrive from those who merely survive.

This kind of knowledge doesn't come overnight, and it certainly doesn’t come without effort. But for those willing to put in the time to educate themselves, the rewards can be significant. The reality is that the more you understand about a particular industry or financial model, the less reliant you become on having cash at the outset. Knowledge is the ultimate investment that grows over time, yielding dividends in the form of smart decisions, calculated risks, and well-structured deals.

Leveraging Resources: It’s Not Just About Your Money

A crucial part of building wealth is learning how to use resources that don’t belong to you—an art many successful individuals have perfected. In many industries, it’s common for entrepreneurs and investors to secure funding not by using their own money, but by seeking out investors, forming partnerships, or accessing loans.

This approach makes sense because it allows individuals to take calculated risks without exposing their personal capital. But, to successfully attract outside investment or loans, you need more than just a good idea—you need a solid understanding of the market and a network of connections. Here, again, knowledge is your best friend. When you can show potential partners or investors that you deeply understand the business and can offer something of value, it becomes easier to gain their trust and support.

In fact, this method of using other people's money is a core principle in the financial strategies of many thriving businesses. Whether it's seeking venture capital or structuring a deal that offers equity in exchange for funding, knowing how to access and utilize resources beyond your own wallet is key.

Why This Approach Matters Today?

We are living in an age where the economic environment is unpredictable. Rising inflation, uncertain markets, and increasing living costs make it difficult for many people to believe they can ever get ahead financially. But it’s precisely in these challenging times that a shift in mindset becomes most crucial.

Instead of focusing on the barriers, like lack of capital, the focus should be on what we can control—what we know and how we apply it. Financial literacy and understanding are more accessible than ever before, thanks to the wealth of resources available online and through communities of like-minded individuals. By shifting the emphasis from needing money to needing knowledge, anyone can begin their journey toward financial independence.

The power of this mindset lies in its flexibility. Regardless of where you start—whether you have little or no money—you can always start with your mind. You can always learn, always strategize, and always seek out opportunities. The barriers of the past, which often limited those without significant capital from participating in wealth-building activities, are less significant when knowledge is the cornerstone of your investment.

Building Wealth Starts with Belief

Ultimately, the path to building wealth is not about the money you start with. It’s about the mindset you cultivate. It’s about having the confidence to recognize that your most valuable asset is what you know and how you apply it. You don’t need to wait until you have a large sum of money to begin investing or to start a business. What you need is a strategy, a plan, and the willingness to continuously educate yourself.

In the end, building wealth is a mental game. It’s about positioning yourself mentally before you position yourself financially. Whether you’re leveraging other people's money or making smart, informed decisions, success starts in the mind. The earlier we embrace this reality, the sooner we can transform our financial futures, one strategic step at a time.

Read other articles by following this link http://amazingartnet.blogspot.com/2024/10/breaking-free-from-friendzone.html

Address

Chileka
<<NOT-APPLICABLE>>

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Amazing Art Network posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Videos

Share


Other Chileka media companies

Show All