Second half blue eagles vs Bullets live
Malawi payekha nkovuta kuthetsa corruption coz no corruption zinthu zifika pa worse .
Muone maiko olemela corruption sinkhani only let's build our country with strong idears. Like kutsitsa zinthu zofunikila kwambiri like chakudya then fertilizer apo basi Malawi watheka koma tikapimbana kwambiri ndi corruption iswear Malawi afika povetsa chisoni .
Azimangidwa inde but do you think this government mulibe corruption??
I heard Acb last time akuti this government it's worse corruption.
Chomwe chikutunika ndi kumupanga malawi akhale wabwino Koma to deal with corruption hmmmm tichedwa zikukanika kutha corruption maiko olemera malawi nchiyaniso ? Corruption singathe koma tikungosintha opanga corruption wo basi .
Tikapanda kusamala dziko ilili lifika polilitsa umphawi, chifukwa tikulimbana ndizoti sizingatheke ndipo singathe corruption ndiye tikuchedwanazo nthawi ikutha tili busy ndi zosatha .
Bweletsani fertilizer komaso chakudya chikhale pa size yabwino muzaona zinthu kkuyenda mwabwino kwambiri .
Or atamaba koma Malawi Eni nthaka akusangalala zilibe ntchito bola enidziko sakuvutika .
Bingu adakwanitsa kuchepetsa njala mmalawi momuno do you think iye komaso anthu ena samaba?
Vuto panopa Malawi tikudandaula kuwili
Aboma akuba plus leadership 0% amalawi akuvutika , pamenepo ndiye oba mu bomawo amaonekera mwachangu .
Malawi safuna zambiri ayi msima yokha nkhani yatha.
Signed by
#Yathu