Trevor Records Inc

Trevor Records Inc This is the page that thrives to unearth and promote local talent among artists. It highlights perso

10/04/2024

Ice Kid X Big Lil Stain~(prod El_Clin)
Trevor Records Inc
Highlight
Everyone

 πŸ˜­πŸ˜­πŸ˜­πŸ’”SAD :   Chiwerengero cha anthu omwe amwalira kwa Manase ku Blantyre kaamba komwa mowa womwe ukuganiziridwa kuti ndi...
08/04/2024

πŸ˜­πŸ˜­πŸ˜­πŸ’”SAD
:

Chiwerengero cha anthu omwe amwalira kwa Manase ku Blantyre kaamba komwa mowa womwe ukuganiziridwa kuti ndiuja umagulitsidwira m'zigubu wotchedwa 'Ambuye ntengeni' pena 'Magagada' tsopano chafika pa asanu ndi awiri.

Kupatula asanu omwe anamwalira dzulo, Mkulu wa za umoyo mu mzinda wa Blantyre a Gift Kawalazira wati awiri enanso amwalira pa 7 April, ndipo enanso asanu agonekedwa ku chipatala Queen Elizabeth Central komwe akulandira thandizo.

Mu uthenga womwe atulutsa, a Kawalazira ati mwa zizindikiro zina, anthuwo akumavutika kupuma, akumatsegula m'mimba, kusaona bwino komanso kumva kuphwanya thupi.

Zoyeza za limodzi mwa matupi a omwe adamwalira zikusonyeza kuti mthupi mwawo munali mankhwala akupha (poison).

Pakadali pano iwo achenjeza anthu m'dziko muno kuti apewe kumwa mowa wosadziwika bwino komanso wosavomerezeka.

:
(Wolemba Mathews Kasanda)

05/04/2024




πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯
EveryoEveryoneiHighlightrTrevor Records Inc

Heroes get remembered, but legends never die but they multiply. Continue resting in power our Legend  ✊ Everyone
05/04/2024

Heroes get remembered, but legends never die but they multiply. Continue resting in power our Legend ✊

Everyone

06/10/2023

πŸ”₯πŸ”₯Amkayesa Andikwilira Video Lyrics

Rest in peace Andy Spice (Twin M)😭😭😭Mzimu wako uwuse mu mtendereπŸ’”πŸ’”πŸ˜­πŸ˜­
07/04/2023

Rest in peace Andy Spice (Twin M)😭😭😭
Mzimu wako uwuse mu mtendereπŸ’”πŸ’”πŸ˜­πŸ˜­

Address

16 Nzeru Drive Road, Nancholi
Blantyre

Telephone

+265995212324

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Trevor Records Inc posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Videos

Share

Category