Oracle News and Talks

Oracle News and Talks Certified Journalist,PR Marketer and Entrepreneur.

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Kaitano Kalion, Mana Tiksy Chiwalo, Mercy Masanga, Chikum...
03/04/2024

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Kaitano Kalion, Mana Tiksy Chiwalo, Mercy Masanga, Chikumbutso Wilson, Emmanuel Continhu Malunga, Star Bouy Brihzah, Remxon Freod, Dyson Layelo

23/12/2023

Ma born again ambiri samasiyanitsa kulungama ndi kupepera😂

Utha kumaona ngati ukulungama ukupepera😂

Ndatchula munthu?Amene imukwane aivale ndi yake😂

22/12/2023

Osalora kulangizidwa ndi aliyense,adani amatha kukulangiza ndipo malangizo ena ndi opanda nzeru

Yamukwana aivale ndi yake.😂

20/12/2023

Enanu tinakupasani cross koma si mwano wake nonse pano,ati wachitatu osokonedza,Aaaa ineyo or ndasanduka Satana lero?😂

Muzandifuna imukwane ndi yake aivale bas😂

Send me your CV mpaka 5 years,ankolo  pena pake mukulakwisatu😂😂
20/12/2023

Send me your CV mpaka 5 years,ankolo pena pake mukulakwisatu😂😂

19/12/2023

Ati am proud Catholic aaaaa iwe😂😂😂

Bwerani pano mutiuze k*t zik*t bwanj😂

# iyi yokha ndi size yanu ivaleni😹

18/12/2023

Munthu ukusungidwa and zikukuvutanso,chopelekera mimba ndi chaninso abale?💔 Anthu ena mavuto mumachita chowatokosola dala😂

16/12/2023

Ma affliates akangovota mwa chamba amenyedwa lero😂😂winayu anthu sakumufuna😂

It's true that betrayal doesn't come from an enemy,this dude Amos took part pokupha mlongo wake Agnes Katengeza.Munthu y...
14/12/2023

It's true that betrayal doesn't come from an enemy,this dude Amos took part pokupha mlongo wake Agnes Katengeza.Munthu yemwe ankamusunga mmalo momubwezera ulemu nkumupha😰,anthu ena are ungrateful and masiku ano achibale ambiri akuopsa kuposa nkango.Mzimu wa Agnes upitilize kuwusa mu mtendere.

25/11/2023

Even mwana opanda khalidwe akalemera amakhala chitsanzo Cha bwino🚶

24/10/2023

Tsogolo la wina aliyense liri mmanja Mulungu ❤️

23/10/2023

Kukhala ndi moyo ndi Testimony 😊

16/10/2023

Ngakhale Paulo amamunena k*ti sakukwatira sizinatsithebe kanthu sanakwatire 😂😂

Government Introduces Special Allowance package to all its Civil Servants effective October 1st,2023 aiming to improve t...
25/09/2023

Government Introduces Special Allowance package to all its Civil Servants effective October 1st,2023 aiming to improve their livelihood.

High Court Judge Redson Kapindu has ruled that the Anti-Corruption Bureau (ACB) should give all its evidence to Vice Pre...
25/09/2023

High Court Judge Redson Kapindu has ruled that the Anti-Corruption Bureau (ACB) should give all its evidence to Vice President Saulos Chilima’s defence team before he can take plea in the Zuneth Sattar-related corruption case.

Chilima is this morning appearing before the court for the case, in which he is charged with three counts of corruption for allegedly receiving a $280,000 bribe from businessperson Zuneth Sattar to secure government contracts.

Kapindu made the ruling this morning ahead of Chilima’s second plea, following amendment of the charge sheet by the State.

The ruling has quashed the ACB’s earlier submission that it could not submit some of its evidence because of its sensitive nature.

The court, however, has ruled that the ACB should not disclose its investigation report as it is not important to the case.

*Oracle*

22/09/2023

Kumalimbikira xul ndi hustle,anzanu akusowa ma opportunities ngat anuwo,that should be you're advantage.Nzopweteka kukulira ku family yoiphuira kuzafa kape makolo kulibe Kapena Makolo azakuone ukuvutika Mmalo Moti uwandize👌

Bwalo lamilandu lavomela mapempho onse a Bon Kalindo oti bwaloli lichotse kalata yopeleka chilolezo kwa a polisi k*ti aw...
19/09/2023

Bwalo lamilandu lavomela mapempho onse a Bon Kalindo oti bwaloli lichotse kalata yopeleka chilolezo kwa a polisi k*ti awamange komanso k*ti bwaloli lisachotse belo yawo monga a polisi amafunira.

Popeleka chigamulochi, Senior Resident Magistrate Wanangwa Nyirenda wadzudzula apolisi posatsata malamulo powamanga a Kalindo.Pa chifukwa ichi bwaloli lagamula k*ti akalindo awamasule.

Malingana ndi a Nyirenda palibe umboni okwanira omwe mbali ya boma yaonetsa mu bwaloli k*ti a polisi anawaonetsa a Kalindo kalata yowamangira ndi zifukwa zake pa nthawi yomwe amawamanga.

Bwaloli lati malinga ndi malamulo apolisi amayenera kuwatengera a Kalindo Ku bwalo lamilandu pa nthawi yomwe anawamanga osati kukawasunga ku polisi yak*tali ya Ntakataka.

*Oracle*

Address

Oraclekalulu@gmail. Com
Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Oracle News and Talks posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share