Malawi News 24hrs

Malawi News 24hrs Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Malawi News 24hrs, Mugabe Highway, Blantyre.

KATHYALI UYUKoma azimayi🤦🏻‍♂️Nkulu mukumuona apayu wamangidwa akuti amabela azimayi pa Facebook pomawanamiza kuti amawak...
05/01/2024

KATHYALI UYU

Koma azimayi🤦🏻‍♂️

Nkulu mukumuona apayu wamangidwa akuti amabela azimayi pa Facebook pomawanamiza kuti amawakonda, amatumiza friend request kenako akamuvomela amailowa kumawauza kuti awakonda ndipo azawakwatira zikatelo amakumana kuma room basi nzimayi akangoti zungulili iyeyu amatola ma phone basitu uyoooo wautali.

So far wabelako azimayi 7 koma tsoka ndilo amumbwandira🤦🏻‍♂️

MIJBanja lina lakufuna kwabwino dzulo usiku linamchotsa Hendrina Kamenya ku likulu laboma munzinda wa Lilongwe pamene am...
05/01/2024

MIJ

Banja lina lakufuna kwabwino dzulo usiku linamchotsa Hendrina Kamenya ku likulu laboma munzinda wa Lilongwe pamene amapanga m'bindikiro wake wofuna kuti ampatse ndalama zamalemu Bambo ake.

Nkhani ya Hendrina dzulo lonse yakhala ikukambidwa pamene akufuna ndalama zamalemu Bambo ake kuti akapangile maphunziro aukachenjede.

Ndipo usiku Hendrina anapitiriza kukhala pama ofesi a Accountant General ngakhale kuti kunja kunali kukugwa mvula.

Izi ena atawona kuphatikizapo mmodzi mwa aphungu a DPP Mary Navicha pamodzi ndimkulu womenyela ufulu anthu Levi Lwemba anapita Ku Capitol Hill usiku kuti akamchotseko mstikanayu kutengera kuti ndimalo oopsa komanso kunali mvula.

Poyankhula ndi MIJ Online Navicha, yemwe ndimtsogoleri wa amai mchipani cha DPP wati anakhudzidwa kwambiri atawona nkhaniyi ndipo anafuna kuti ngati kholo akamsunge kaye kwawo koma mwamwai banja lina lakufuna kwabwino lamchotsako Hendrina Ku Capitol Hill.

Navicha walonjeza kuti mmasiku ochepa achititsa zionetsero kuti amai ndi ana omwe nawo ndalama zawo zikuvuta kupelekedwa ayankhule mawu amodzi ndicholinga choti Boma liwathandize kuti apewe mavuto omwe akukumana nawo.
-Malumbo Ngwira-

15 FACTS ABOUT KENDALL KAMWENDO1. Born in Chirimba (Blantyre), Kendall Zivile Kamwendo is currently aged 42.2. He is the...
04/01/2024

15 FACTS ABOUT KENDALL KAMWENDO

1. Born in Chirimba (Blantyre), Kendall Zivile Kamwendo is currently aged 42.

2. He is the last born in a family of three.

3. He originally comes from Dowa and Ntcheu districts where mother and father originally came from.

4. He met Symon Kamlaka after his relocation to Area 25 (Lilongwe) in the very late 1990s. They shared neighbourhood.

5. Kendall and Symon released their very first single titled Nyemba Nyemba in 2003 and later composed debut album whose album track was the aforementioned single.

6. He did his secondary education at Kabwabwa in Lilongwe.

7. Kendall holds Diploma in Accounting and Advanced Certificate in Information Processing of City and Guilds.

8. Kendall had worked in the civil service for about 14 years specifically as an accountant in the local government and Ministry of Lands before quitting to concentrate on his ownership of Luso TV.

9. He was the founder of Luso Television that was closed some years ago because of financial challenges.

10. He has a number of businesses. For example, he is the owner of Zivile Buses.

11. He got married to Konde in 2010. The couple has children. One of the children is the first-born daughter named Faith who appeared in the film Where My Heart Belongs. The daughter is currently aged about 13 years.

12. Kendall is a christian. He belongs to Church of Central African Presbyterian (CCAP).

13. He also has drinking joint and timber-cutting and selling company in Chikangawa Forest.

14. Apart from being a musician and businessperson, Kendall is a film actor, script writer, director and producer. In addition to Where My Heart Belongs, Kendall has also starred in, directed and produced the newly released trending movie titled School Days.

15. He says he has intentions of vying for parliamentary seat someday.

>Compiled by Blessings Chimkango

04/01/2024

Just In:

Man of the moment Dr Kondwani Nankhumwa MP and Leader of Opposition in Parliament has arrived at Golden Peacock in LILONGWE for a disciplinary hearing.

Nankhumwa is one politician whose name is everywhere in the country.
Wishing him well.

People's choice!
Proudly known as KN.


04/01/2024

Macheza:::

TYPES OF SCAMS IN MALAWI 🇲🇼😏

1. Send me your CV - Scam.

2. We'll get back to you - Scam.

3. I love you more than I love my wife - Scam.

4. Police is your friend - Scam.

5 The youths are the future leaders - Scam.

6. Airtel Data bundles - Scam.

7. Your vote counts - Scam.

8. Send me money to visit you - Scam.

9. I have a boyfriend but it's complicated - Double Scam.

10. This is not a scam - Scam.

11. Our school is the best - Scam.

12. Come over I want to show you
something - Scam.

13. Oh, he’s just a childhood friend - Scam.

14. He's like a brother to me - Outstanding Scam.

15. I'm with the boys - Scam

15. I promise I won't tell anyone - Scam.

16. I saw you in my dreams giving you a ring - Pure Scam.

18. A: Lets do a video call...
B: Sorry my network is bad, my battery is low, my room is dark - Chief Scam

19. This year I see you buying a car - Spiritual Scam

20. Baby, you are the most beautiful girl I have ever seen - 5G Scam.

21. Why didn’t I meet you before marrying my wife? -Scammest Scam of them all.

Bonus scam!!!

22. I have never loved someone like this before - Greatest Scam
23. We are just friends - SCAM
24. Tonse alliance - National Scam

In fact, you're all SCAMMERS!
@followerslipo ndithu!

Just InFrom the office of Leader of Opposition in Parliament Dr Kondwani Nankhumwa MP.
03/01/2024

Just In

From the office of Leader of Opposition in Parliament Dr Kondwani Nankhumwa MP.


Just inMulli holds prayers at his headquarters in Chigumula Blantyre.MBL Holdings held prayers at Chigumula township of ...
03/01/2024

Just in

Mulli holds prayers at his headquarters in Chigumula Blantyre.

MBL Holdings held prayers at Chigumula township of Blantyre today on 03/01/2023.
Present at the function were Rev Dr Billy Gama,Rev.Father Boniface Tamani and Father Mthalika.


03/01/2024

*MBL HOLDINGS YACHITITSA MAPEMPHERO LERO KU CHIGUMULA NDI MABOMA ONSE KOMWE KULI MAKAMPANI AWO*

Mulli Brothers Limited (MBL) Holdings yemwe mwini wake ndi a Leston Ted Mulli achititsa mapemphero ku Chigumula mu nzinda wa Blantyre komanso maboma onse omwe kuli makampani awo muno mMalawi.

Mutu wa mapemphero a lero udali; *Kupempherera mabuzinesi awo kuti ayende chitsogolo pamene akukomana ndi mavuto osiyasiyana.*

Mmawu awo mkulu woyang'anira zintchito ku MBL Holdings bambo Joseph Khupe apempha boma kuti asiye kuikapo ndale pa zakaperekedwe ka ntchito kapena makontarakiti akayendetsedwe ka mabuzinesi mdziko muno ndipo adapitiliza kunena kuti makampani a MBL Holdings ali ndi anthu ambiri omwe adawalemba ntchito zomwe ndi mbali imodzi yothandizira kutukula dziko lino.

Kuthirapo demanga a Rev.Dr. Billy Gama nawo apempha boma kuti kuyambira chaka chino a Mulli akueyenera apatsidwe mabuzinesi kuti dziko lino lipite chitsogolo kumbali yokweza chuma chathu.

A Leston Ted Mulli ali ndi ukadaulo pa nkhani yobweretsa zipangizo zotsika mtengo(AIP) kamba koti ali zonse zoyenereza monga magalimoto akuluakulu omwe angathe kunyamula feteleza kupititsa madera osiyasiyana.

Ena mwa omwe alalikira pa mapempherowa ndi Father Elizeo Mtharika komanso Father Boniface Tamani omwe alimbikitsa a Mulli kuti apilire pamene akukomana ndi zophyinja zambiri.

A Mulli ali ndi makampani okwana pafupi pafupi makumi awiri ndi anayi (24).

Just In:Blantyre MalawiA beautiful city to stay in.
03/01/2024

Just In:

Blantyre Malawi
A beautiful city to stay in.


MBL HOLDINGS  YAKONZA MAPEMPHERO KU CHIGUMULA.Mulli Brothers Limited (MBL) Holdings yemwe mwina wake ndi a Leston Ted Mu...
03/01/2024

MBL HOLDINGS YAKONZA MAPEMPHERO KU CHIGUMULA.

Mulli Brothers Limited (MBL) Holdings yemwe mwina wake ndi a Leston Ted Mulli akonza mapemphero lero pa 03/01/2024, ku likulu (Headquarters) la makampani awo ku Chigumula mu nzinda wa Blantyre.

Cholinga cha mapempherowa ndikuthokoza Mulungu chifukwa cha Chaka cha 2023 ndikupempha madalitso ndi mlozo wa Mlungu mchaka cha 2024.

Anthu azipembezo zosiyanisiyana ndi omwe akutenga nawo gawo pa zochitikazi.

Akutsogolera mapempherowa ndi Rev.Billy Gama.

Just In:::Mvula ya mphavu yagwetsa mpanda wa msika wa Kasungu pafupi ndi banki ya FDH.Malipoti akusonyeza kuti katundu w...
02/01/2024

Just In:::

Mvula ya mphavu yagwetsa mpanda wa msika wa Kasungu pafupi ndi banki ya FDH.

Malipoti akusonyeza kuti katundu wambiri waonongeka ndi mvulayi.


02/01/2024

Just In:
Amen!
Thank God!
Ochita zisudzo mdziko la Nigeria Mr IBU avina molapitsa pa msonkhano wa mapemphero a Mneneri Shepherd Bushiri.

Mr IBU wachira
Ambuye atamandike!
Mr IBU wagonetsa anthu ku Cross Over!

Just In::TIKUGONERA NSIMA YA MADEYA KULI KUSOWA KWA CHIMANGA.Tachilowa chaka cha 2024 koma movutikira momwemu pamene ant...
02/01/2024

Just In::

TIKUGONERA NSIMA YA MADEYA KULI KUSOWA KWA CHIMANGA.

Tachilowa chaka cha 2024 koma movutikira momwemu pamene anthu ambiri alibe chimanga kutsatira kusowa kwa ndalama.

Devaluation yomwe idachitika ija mayankho ake tiyamba kuwaona.
Mavuto anjala akhuza madera ambiri mdziko muno kamba ka ulamuliro wa kagulu kokhako Kali pafupi ndi bwanakhubwa.

Kuchita masewera tifa ambiri miyezi ikubwerayi,mvula yayamba mochedwa zomwe zapangitsa kuti mbewu zizifa ndi dzuwa.

Mkati mkati mwa ulendo opita ku Khenani.


.

Just In *MP CHITSULO AKONDWERERA NYUWERE NDI ANTHU AKE.*Dzulo pa 1 January 2024 , Phungu wakunyumba ya Malamulo wadela l...
02/01/2024

Just In

*MP CHITSULO AKONDWERERA NYUWERE NDI ANTHU AKE.*

Dzulo pa 1 January 2024 , Phungu wakunyumba ya Malamulo wadela la Mwanza West Constituency , Wolemekezeka a Mayi Joyce Chitsulo MP anachititsa chikondwerelo cha chaka chatsopano ( Nyuwele). Mwambowu unachitikila pa Headquarters ya a Senior TA Nthache mubomali. Apatu , Wolemekezeka a Joyce Chitsulo pamodzi ndi anthu awo anakhala pansi kwinaku akuonelela Gulewamkulu .

Nyuwele yinakoma ku Mwanza.

Joyce Chitsulo 2025 Boma!


.

Just In:DZIKO LA ISRAEL LAMANGA NYAMATA WINA YEMWE ANAPITA KUKAGWIRA NTCHITO ZAKUMA FARM KAAMBA KOGWILIRA MZUNGUApolice ...
02/01/2024

Just In:

DZIKO LA ISRAEL LAMANGA NYAMATA WINA YEMWE ANAPITA KUKAGWIRA NTCHITO ZAKUMA FARM KAAMBA KOGWILIRA MZUNGU

Apolice mudziko la Israel agwira ndikusekela muchitokosi nyamata wina ochokera kudziko lino la Malawi pomuganjzila kuti anagwilira mzungu wina waku Israel komweko.

Tibwela ndi nkhani yonse kuphakizapo zithunzi masanawa.


Just InWapha mzake kamba ka k90.000 ku Dowa.Mkulu uyu ndi Yotamu Fulatiya munthu oipa.😭😭😭😭😭
01/01/2024

Just In

Wapha mzake kamba ka k90.000 ku Dowa.
Mkulu uyu ndi Yotamu Fulatiya munthu oipa.
😭😭😭😭😭


Just In:AKWANITSA ZAKA 100 LERO PA 1 JANUARY 2024.Bambo Ephraim Mjiva Mnthali omwe anabadwa pa 1 January 1924 lero akwan...
01/01/2024

Just In:

AKWANITSA ZAKA 100 LERO PA 1 JANUARY 2024.

Bambo Ephraim Mjiva Mnthali omwe anabadwa pa 1 January 1924 lero akwanitsa zaka 100.

Mwambo wachikondwelero ukuchitikira ku Luzi kwa Mfumu yayikulu Jalavikuba boma la Mzimba.


Just In::NANYONI WADZIDZIMUTSA ANTHU NDI MAONEKEDWE AKE APHULIPHULI.Loweluka lapitali ku BICC kunali mwambo opereka mpho...
01/01/2024

Just In::

NANYONI WADZIDZIMUTSA ANTHU NDI MAONEKEDWE AKE APHULIPHULI.

Loweluka lapitali ku BICC kunali mwambo opereka mphoto wa anthu omwe asangalatsa mu chaka cha 2023.

Mai Enifa Chiwaya omwe amatchuka ndi dzina loti NANYONI anadzidximutsa anthu ndimaonekedwe awo aphuliphuli kusiyana ndi mmene amaonekera ma filimu kapena pa canema.

NANYONI anatchena molapitsa zomwe anthu anadodoma kuti uyudi ndi NANYONI wa pa majiga uja.

Ndie amayenda ngati wagwetsa kopa uku akukatenga ma awards ake awiri kamba kokhala msangalatsi kuposa onse ochita zisudzo.

Congratulations NANYONI!
Mumatha achee!


01/01/2024

Just In:

Happy and Prosperous New Year to Y'all.

Ndinu anthu abwino heavy ndipo pitilizani kutsatira page ino ya Malawi News 24hrs.

Timalemba nkhani zokhazo zili ndi umboni.
Ndale komanso zachitukuko ndie kudya kwathu.

Tipatseni nkhani za kwanuko kaya ndinu a shadow MP.

Malawi first.


.

Just InChikho cha Hon Eric Mofolo chaseweredwa masana alero pa bwalo la K_Ground ku Bangwe mu nzinda wa Blantyre.Timu ya...
31/12/2023

Just In

Chikho cha Hon Eric Mofolo chaseweredwa masana alero pa bwalo la K_Ground ku Bangwe mu nzinda wa Blantyre.

Timu ya Mpoza FC yapambaza mwankhanza timu ya Black stars FC pogoletsa zigoli ziwiri kwa duuu.

Hon Eric Mofolo akhale akubweretsa ma Bonanza ankhani nkhani mu cha chomwe chikubwerachi ngati njira imodzi yowapatsa chochita achinyamata mudera.

A Mofolo alinso ndi masompheya odzaima ngati Phungu wa Bangwe Constituency mu 2025.



Just In:::Tsiku lomaliza muchaka cha 2023.Tiyeni timupatse ulemu Phungu uyu wa Blantyre South East Sameer Suleman.Watidz...
31/12/2023

Just In:::

Tsiku lomaliza muchaka cha 2023.
Tiyeni timupatse ulemu Phungu uyu wa Blantyre South East Sameer Suleman.

Watidziwitsa kuti boma la MCP lidabetsa ndalama ku Butchery ndi ku Pharmacy kufuna kugula fertilizer.

Mu Malawi weniweni akuenera kupereka ulemu kwa Sammy's.

Chairperson wa Agriculture ku Parliament.

Ife a Malawi News 24 hrs tikuti Chaka ichi mupangenso chimodximodzi.


*A NANKHUMWA AKHALA NAWO PA MWAMBO WOTSANZIKANA NDI M'BUSA VICTOR MANKHWALA KU PHALOMBE.*Mtsogoleri wa zipani  zotsutsa ...
31/12/2023

*A NANKHUMWA AKHALA NAWO PA MWAMBO WOTSANZIKANA NDI M'BUSA VICTOR MANKHWALA KU PHALOMBE.*

Mtsogoleri wa zipani zotsutsa boma ku nyumba ya malamulo wolemekezeka Dr Kondwani Nankhumwa la mulungu pa 31/12/2023, anali mlendo wolemekeza pa mwambo wa mapemphero otsanzikana ndi m'busa Victor Mankhwala ku mpingo wa Migowi CCAP.

M'busa Mankhwala akuchoka ku mpingowu komwe akhala akutumikira kwa zaka zisanu.

M'busa Mankhwala akupita ku mpingo wa Chitsime omwe uli ku Machinjiri mu nzinda wa Blantyre.

Mmawu awo, a Nankhumwa ayamikira M'busa Mankhwala kamba kotumikira nkhosa za pa mpingowu kwa zaka zochuluka.

Pa za njala yomwe yabuka mdziko iwo ati boma la Phalombe ndi limodzi mwa maboma omwe akhudzidwa kwambiri ndi njala kamba ka Namondwe wa Freddy yemwe adakhuza delari ndipo anapitiliza kupempha Mulungu kuti zomwe zidachitika mu Chaka Cha 2023 zisachitikenso.

M'busa Mankhwala ndi akulu akulu ampingowu ayamikira a Nankhumwa chifukwa cha kuzichepetsa kwawo ndipo ati si chinthu chophweka kukhala ndi mlendo wolemekezeka ngati Dr Kondwani Nankhumwa pa mwambo woterewu.

Pa mwambowu panabweranso mamembala a chipani cha DPP monga a District gavalana mai Rose Makoloni, Constituency gavalana a Phalombe North East a Rodrick Mpoya ndi ena ambiri.

Paramount Chief Kaduya anali nawonso pa mwambowu.

Just In:Phalombe.Lero akhrisitu a mpingo wa  Migowi CCAP m'boma la Phalombe, akusanzikana ndi abusa awo a Reverend Victo...
31/12/2023

Just In:
Phalombe.

Lero akhrisitu a mpingo wa Migowi CCAP m'boma la Phalombe, akusanzikana ndi abusa awo a Reverend Victor Mankhwala omwe tsopano azikatumikira pa mpingo wa Chitsime CCAP ku Machinjiri m'boma la Blantyre.

Mtsogoleri wambali yotsusa boma ku nyumba ya malamulo Dr Kondwani Nankhumwa ndi mlendo wolemekezeka pa mwambowu ndipo afika kale.

Reverend Makhwala atumikira pa mpingowu kwa zaka zisanu.

Mamembala achipani cha DPP omwe awaperekeza Dr Kondwani Nankhumwa ndi district gavanala Mai Rose Makoloni, Constituency gavanala bambo Rodrick Mpoya ndi ena ambiri.

Paramount Chief Kaduya alinawo pa mwambowu.



The Transporters Association of Malawi (TAM), a grouping of leading Transporters of Dry and Wet cargo in and outside the...
30/12/2023

The Transporters Association of Malawi (TAM), a grouping of leading Transporters of Dry and Wet cargo in and outside the country, has announced the commencement of an initiative of providing fuel to all trucks transporting fertilizer in the Northern, Central and Southern Regions of Malawi starting from today for the speedy transportation of fertilizer.

TAM which is in a contract with Ministry of Agriculture under Smallholder Farmers Fertilizer Revolving Fund of Malawi (SFFRFM) has taken the initiative to ensure that there is no interruption in supply of the commodity in all the districts.

"The Association believes doing so will help Malawi government to help the less privileged farmers timely access to the Affordable fertilizer under the AIP as the rains have stabilised almost in all parts of Malawi," says Frank Banda, TAM Spokesperson.

Meanwhile authorities at TAM have appealed to all Transporters, truck owners and operators to prioritize carrying fertilizer under this program in order to support the agriculture sector in the country.

Banda has added that TAM has committed to ensuring that all the beneficiaries redeem fertilizer on time.

Despite most parts of the country receiving rains, some beneficiaries are yet to get the items.

Just In:Mwini wake wa Thuchira Tourist Lodge muboma la Phalombe wakonza show ya oimba osiyana siyana mawa pa 31 Dec ndi ...
30/12/2023

Just In:

Mwini wake wa Thuchira Tourist Lodge muboma la Phalombe wakonza show ya oimba osiyana siyana mawa pa 31 Dec ndi pa 1 January ngati njira imodzi yokondwerera kutha kwa Chaka komanso kuyamba kwa Chaka china.

Ndipo show yi ndiyaulere.
Tiyeni Tiyeni Tiyeni kwa ife okhala ku Mulanje, Thyolo Komanso Chiradzulu.


Just InBreaking News:Prophet Christopher Phiri wa mpingo wa Supernatural Embassy Ministry, m'boma la Mangochi, amulamula...
29/12/2023

Just In

Breaking News:

Prophet Christopher Phiri wa mpingo wa Supernatural Embassy Ministry, m'boma la Mangochi, amulamula kuti akagwire ntchito ya kalavulagaga kwa zaka 19 chifukwa chopezeka wolakwa pochita chigololo ndi mwana wobereka yekha wa zaka 16.


Just In:BOMA LAUMBAVA ILI:Malipilo ku Israel: boma lati amene sakufuna asiye, apeleke mwayi kwa enaPomwe pali kusamvana ...
29/12/2023

Just In:

BOMA LAUMBAVA ILI:

Malipilo ku Israel: boma lati amene sakufuna asiye, apeleke mwayi kwa ena

Pomwe pali kusamvana pa nkhani yamalipiro pakati pa achinyamata omwe akugwira ntchito mdziko la Israel ndi ma agent omwe adawatumiza mdzikolo, boma kudzera mwa Kazembe woimila Malawi ku Israel lati achinyamata omwe sakufuna kuti ndalama zawo zidzilowa ku banki, anene ndipo ndege yowabweletsa kuno kumpanje ilipo kale.


.

29/12/2023

Just In:::

That's the video of Vin and his friends.

Vin is currently in hospital receiving medical treatment.
Zinjoyi ziphetsa!

Watch it till the end.

Malawi News 24hrs keeping you posted.


*UTSOGOLERI*Mu chithunzi mukuchionachi omwe akhala pansiwo ndi wolemekezeka Dr Kondwani Nankhumwa. Pa nthawiyi nkuti aku...
29/12/2023

*UTSOGOLERI*

Mu chithunzi mukuchionachi omwe akhala pansiwo ndi wolemekezeka Dr Kondwani Nankhumwa. Pa nthawiyi nkuti akugwira ntchito ku bungwe la Malawi Broadcasting Corporation (MBC).

Mukuona chani mu chithunzi chimenechi?Mukuphunzirapo chani pamenepa?

Mwachidule, apa m***a kuona kuti mphatso ya utsogoleri mwa Dr Kondwani Nankhumwa idayamba kale kale.

Utsogoleri ndi mphatso yochokera kwa Namalenga.

Tiyeni timupatse support yochuluka kuti dziko ili aliphule pa moto omwe tilinawowu.


Just In::WACHOTSEDWA GANYU KU STATE HOUSE.Tiyanjane,mtsikana weniweni wa chipani cha MCP wachotsedwa ntchito ku nyumba y...
28/12/2023

Just In::

WACHOTSEDWA GANYU KU STATE HOUSE.

Tiyanjane,mtsikana weniweni wa chipani cha MCP wachotsedwa ntchito ku nyumba ya chifumu kamba koulura zinsisi za anthu omwe akuba mudzina la MCP.

Tiyanjane Mlangeni masiku apitawo adatulutsa ma VN omwe watafulira ena mwa anthu akuchita katangale ooopsya kwambiri mudzina la Kongeresi.

Boma ili itipha ikuba too much watero Tiya.

Mkati mkati mwa ulendo opita ku Khenani.


Just In:::😭😭😭😭A Luciano Brighton omwe adali phunzitsi wa Pulayimale sukulu Ina muboma la Mwanza azimangirira kamba ka ma...
28/12/2023

Just In:::

😭😭😭😭
A Luciano Brighton omwe adali phunzitsi wa Pulayimale sukulu Ina muboma la Mwanza azimangirira kamba ka mavuto azachuma omwe akuta dziko lino.

A Brighton apezeka atafa mnyumba mwawo lero pogwiritsa ntchito neti yaudzudzu.

Mzimu wawo ukause mumtendere.

28/12/2023

Ku Israel Mayooo



Kusamvana pa nkhani yamalipiro kwabuka ku Israel pakati pa achinyamata omwe akugwira ntchito zakuminda ndi ma agent omwe adawatumiza mdzikolo.

Times yalankhura ndi ena mwa achinyamatawa omwe akuti, ma agent akuwakakamiza kuti asayinire zikalata zomwe zikusonyeza kuti malipiro awo a pamwezi adzipita kwa ma agent-wo.

"Akuti malipiro athu onse adzipita ku account kwawo kenako iwowo adziwatumiza ku Malawi-ko. Ife izi sitikugwirizana nazo chifukwa ntchito tikugwira ndi ife osati iwowo, ndiye anayenera kutisiyira ndalamazo kuti zizipita ku Malawiko kudzera mma account athu kapena a mabwana athu," atero anyamatawo.

Iwo ati, zomwe zikuchitika ndi ngati kuwagwiritsa ntchito ya ukapolo chifukwa malipiro awo onse adzitumizidwa ku Malawi nkuwasiya iwo opanda ndalama iliyonse ngakhale yogulira sopo.

Iwo adandaulanso kuti adawatengetsa ngongole yokwana USD1,650 (K2,887,500) yomwe adawauza kuti $650 ndi ya ndege ndipo $1000 ndi yoti ikawathandize akakafika ku Israeli.

"$1000 idayikidwa ku ma account athu koma patapita kanthawi ma agent adayitengako ndalamayo kutisiya ife opanda kanthu. Adanama ku Malawiko kuti atigulira ma smartphone ndi ndalama yathu ya ngongoleyo koma sanatigulire. Ndiye tiwapanga trust bwanji ndi salary yathu yonse? Sakufuna kumatigwilitsa thangata awa?" Watero mmodzi wa anyamatawo yemwe pakadali pano wakana kusayina chikalata chomwe wapatsidwa kuti asayine.

Koma mmodzi wa ma agent-wa a Chifundo Banda ati iyi ndi njira yoti ndalamazo zidzifika kuno kumudzi mosavuta chifukwa achinyamatawo sangaitumize ndalamayo mwaokha.

Wolemba Cathy Maulidi

Just In::: *A RALPH JOOMA NDIE MNENERI WA A NANKHUMWA*Mtsogoleri wa mbali yotsutsa boma ku nyumba ya Malamulo wolemekeze...
28/12/2023

Just In:::

*A RALPH JOOMA NDIE MNENERI WA A NANKHUMWA*

Mtsogoleri wa mbali yotsutsa boma ku nyumba ya Malamulo wolemekezeka a Dr. Kondwani Nankhumwa asankha a Ralph Jooma kukhala mneneri wawo.

A Nankhumwa alengeza izi kupyolera mu chikalata chomwe atulutsa lero.

A Jooma ndi Phungu wa chipani cha Democratic Progressive (DPP) ku dera la Mangochi-Monkeybay.


28/12/2023

Just In:::

Umu ndi mmene abale athu akuthamangira kusaka khobiri yomwe adzatiwalire ku mudzi kuno akadzabwera.

Mpata okhala pa Facebook or Whatsapp alibe kkkkk
Slave Trade is real.


Just In:Sitima yatseka mseu wa Machinjiri mu nzinda wa Blantyre madzulo omwe uno kamba ka Network yomwe imagwiritsa ntch...
27/12/2023

Just In:

Sitima yatseka mseu wa Machinjiri mu nzinda wa Blantyre madzulo omwe uno kamba ka Network yomwe imagwiritsa ntchito sitimayi.

Pakadali pano magalimoto ambiri angoima kudikira kuti Network ibweremo ndipo sidzikudziwika kuti ibwera nthawi yanji.

Zangovuta mseu uwu boma limaenera kudutsitsa njanji pansi pake.

Mkati mkati mwa ulendo opita ku Khenani.

Address

Mugabe Highway
Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Malawi News 24hrs posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Videos

Share