Ghetto Got Talent

  • Home
  • Ghetto Got Talent

Ghetto Got Talent Let the talent speak.
(1)

Hi Ndikufuna mkazi wadzaka zosachepela 30 koma akhale opanda mwana . Chifukwa ineso ndilibe mwana .Ndimagwira ntchito ya...
03/02/2025

Hi
Ndikufuna mkazi wadzaka zosachepela 30 koma akhale opanda mwana . Chifukwa ineso ndilibe mwana .Ndimagwira ntchito ya guard .

Police imaphweka ikakhala kuti siikupanga zaiwe..
03/02/2025

Police imaphweka ikakhala kuti siikupanga zaiwe..

03/02/2025

Mbayani ,Chilobwe,Soche,Chirimba,Bangwe,Ndirande,Machinjiri,Lunzu please musagone mbulanda mvula yaonjeza iyi🙌

03/02/2025

Umu ndi mmene zinalili ku Chiwembe ( Blantyre)

Pali mau awa - Madzi saiwala khwawa 🙌

03/02/2025

Madzi adula bridge yaku chiwembe.(Blantyre)

Bridge yomwe yadukayi ndiimene imasiyanitsa pakati pa chiwembe housing ndi chiwembe village...
Ndipo madzi achita kusayeruzika.

Mmene amauzidwa kuti ndichosendera mbatatesi atachimetera kale kawiri...Anthu mulipachangu
03/02/2025

Mmene amauzidwa kuti ndichosendera mbatatesi atachimetera kale kawiri...

Anthu mulipachangu

03/02/2025

Ankolo alalata osati masewera 😂

03/02/2025

Kwini Shaba kokudaidaku zoona kudikuranso cholinga tiyambane ndi azikazathu mmakomomu tikamaonera video yakoyo?

03/02/2025

Ngati mwamutolera wa Bakili Muluzi TV uja ndekuti basi mwadziwano cholinga chake..BMTV inspiring the nationâš¡

03/02/2025

Chichokeren pa 31 December 2024 watulukirano lero akuti ndimukhulukire Koma akungomva mseru 😳

03/02/2025

James Mwanawasa mwaonjeza mpaka kumanyenga mwana wanu yemwe wa zaka 14 mpaka kumupatsa mimba.

Just in BangweBridge ya ku Bangwe madzi akudutsa pa mwamba kamba mvula yomwe yagwa kwambiri ku Blantyre...Ndipo anthu ko...
03/02/2025

Just in
Bangwe

Bridge ya ku Bangwe madzi akudutsa pa mwamba kamba mvula yomwe yagwa kwambiri ku Blantyre...

Ndipo anthu komanso magalimoto akulephera kupita mbali Ina.

Ife omwe taphunzira ma primary aku mudzi komanso amma ghetto tabwerani tiwauze enawa zomwe timkapanga tili ku school..1....
03/02/2025

Ife omwe taphunzira ma primary aku mudzi komanso amma ghetto tabwerani tiwauze enawa zomwe timkapanga tili ku school..

1. Timkalembera ma slet
2.Timkaika mu botolo la covo chimanga chokazinga
3.Timkanyamulira makope mu jumbo la sugar
4.Timkanyamura mbatata ophika,mkumuika mu jumbo la 50 tambala
5.Timkathawa ku school kukatchola ma guava,matutungwa,nkholongo,kadati,mateme,mnyenywe,nchulutsa,malambe,bwemba,misinde(misale),minkhaka,mavembe(water melon) matowi, ndi Zina zambiri.
6.Timkaika freezes wa swana mu malambe
7.Timkagura mbadyira(atondido,kadyaubwerere)
8.Timathawa ku school tikangoona kubwera magalimoto timati opopa magazi.
9.Tikasesa timalembapo dzina lathu kuti lidala akabwera mochedwa adzaone kuti tasesa ndipo amangokopera dzina mukope kuchokera pa bwalo
10.Timamenya ndeu ya by chikuti

Kwinako mumalizitsa...

Ukangoona ana ngati awa umangodziwa kuti si ana aawamba..1. Ku school amapita pa galimoto amawayendetsa ndi driver wa nt...
03/02/2025

Ukangoona ana ngati awa umangodziwa kuti si ana aawamba..

1. Ku school amapita pa galimoto amawayendetsa ndi driver wa ntchito kapena school bus imakawatenga pa khomo ndipo imawakasiya akaweruka.

1.Akamapita ku School amanyamula container ndi pocket money.

3.Fees ndi 2 million kumakwera
4.Ku school kwawo ndi English compulsory

Kwinako malizitsani.. zinazo sitingadziwe tinaphunzira pa Mkolokoti ife.

Izi munalawako?
03/02/2025

Izi munalawako?

Ma legend aona kale in 3 seconds..
03/02/2025

Ma legend aona kale in 3 seconds..

Akazi akaona chonchi mmitima mwao amangomva kukoma ndipo amuna omwe amafuna ndi ngati awa koma zimangovuta kuti oterewa ...
03/02/2025

Akazi akaona chonchi mmitima mwao amangomva kukoma ndipo amuna omwe amafuna ndi ngati awa koma zimangovuta kuti oterewa ndiwochepa..

Anthu musamakhale ndi mwano choncho,mwina angofanana koma si Gwamba ndithu ...
03/02/2025

Anthu musamakhale ndi mwano choncho,mwina angofanana koma si Gwamba ndithu ...

Address


Telephone

+265881217591

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Ghetto Got Talent posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Ghetto Got Talent:

Videos

Shortcuts

  • Address
  • Telephone
  • Alerts
  • Contact The Business
  • Videos
  • Claim ownership or report listing
  • Want your business to be the top-listed Media Company?

Share