13/01/2024
George Qoma yemwe akufuna kupikisana nawo pa mpando wa uphungu kunyumba ya malamulo ayamba ntchito yomanga malo omwe akabaza azikhalapo kuti azikhala otetezeka pa msika wa Nchalo m'boma la Chikwawa.
A Qoma aimira dera la pakati chakuzambwe kwa boma la Chikwawa pa chisankho cha 2025