The Chord TV

The Chord TV Chord Tv, Is Here To Entertain, Educate, Promote Art & spreading the word of God.
(6)

Chord Online Tv, is their to entertain, educate and promote any art to the world. We believe that those artist that do not have a platform to showcase their skills, We should give them a platform to do so. All songs we play on chord tv copyright rights belongs to the owners of the work and all credits are given to the owners.

Apapa koma yafika pa fire, yalowera ku mpaliro, athyolana makosi.Koma yanu mutenga??????
16/01/2025

Apapa koma yafika pa fire, yalowera ku mpaliro, athyolana makosi.
Koma yanu mutenga??????

16/01/2025

ZOPEWEKA PEWANI

16/01/2025

Ku Mulanje, anthu ena amtima wa nkhalamo amene sakudziwika apha mai wa zaka 36, Annie Lajab, powadula khosi.

M'neneri wa polisi ya Mulanje, a Innocent Moses, ati maiwa anapita ku Nkhalango ya Limbuli Teas Estate dzulo komwe amatola nkhuni koma iwo sanabwelerenso kunyumba.

Malemuwa amachokera m'mudzi wa Maliyera mfumu yaikulu Njema m'boma lomweri la Mulanje.

The Democratic Progressive Party (DPP) has appointed Jean Mathanga as National Director of Elections. The appointment is...
16/01/2025

The Democratic Progressive Party (DPP) has appointed Jean Mathanga as National Director of Elections. The appointment is effective January 1st, 2025.

According to DPP Publicity Secretary Shadric Namalomba, the appointment comes after previous elections director Gladys Ganda was reassigned to the job of presidential
adviser.

16/01/2025

Network ikumavuta masiku opanga expire bundle akusendera kuchitseko anthu akunyinyilika nazo, sambi izi.

16/01/2025

Dzulo Kunali ku vavadana, kugwirana nkhwiko kokumbukira chilembwe day kamba kokanganilana msalu za MCP ndi ma T-shirt

16/01/2025

Message yoti Fiber wadukanso ndi kusakhazikika kwa network 🛜 yakupezani kale?
Hmmmmmm

Happy birthday dolo Emmie Deebo
16/01/2025

Happy birthday dolo Emmie Deebo

16/01/2025

Mkazi wawo wapeza ntchito yamasana iwo amagwira usiku akungokumana munsewu daily..iiiii atani?

Njinga ipite koma na pafikapa thumba lachimanga lisale.
16/01/2025

Njinga ipite koma na pafikapa thumba lachimanga lisale.

Ngati angagagade Algeria, Egypt, Comoros, The Gambia, South Africa, and Gabon Ku ma playoffs, Flames ikhoza kupita Ku CH...
16/01/2025

Ngati angagagade Algeria, Egypt, Comoros, The Gambia, South Africa, and Gabon Ku ma playoffs, Flames ikhoza kupita Ku CHAN....

Tsopano pano Boma lavomeleza kuti likudutsa mu mbonawona, likukhomedwa nkhonya pa liwombo inu, akuti likulumidwa ndi msi...
16/01/2025

Tsopano pano Boma lavomeleza kuti likudutsa mu mbonawona, likukhomedwa nkhonya pa liwombo inu, akuti likulumidwa ndi msikizi kamba kamavuto amene likumenyedwa nawo makofi phaaaa, phwaaaaa tibuuuuu.

koma tsopano malingana ndichikalata chomwe boma latulutsa lati zonsezi zikhala nkhambakamwa ndipo zomwe anakambirana ndi a bungwe la PAC atalikhazika pa simba lamva.

Boma lati silinawilingule koma likuyesesa kubweletsa ndondomeko zokoma komanso zokomza kukanthawi kochepa komanso nthawi yayitali kuti zibakhera zimenezi zisazabwelenso.

Zambiri zili mukalata ili munsiyi.

Humble and talented Babra nyangulu chapita. Gospel artist...
16/01/2025

Humble and talented Babra nyangulu chapita. Gospel artist...

Sanafune kuvula suit powoloka pa mtsinje....
16/01/2025

Sanafune kuvula suit powoloka pa mtsinje....

16/01/2025

Mpake akaluza amasekedwa kwambiri mpaka kulira...eee Anjovu ama lubwa akawina,apa Lero sitimwa madzi town mu hmmmm

16/01/2025

Ndinu okoma mtima Yehova mwateteza ife Ku mivi yolusa m'mene tinali mtulo mpaka tadzuka wa moyo.
Mamawa wabwino

Full time Arsenal 2 Vs 1 Tottenham
15/01/2025

Full time

Arsenal 2 Vs 1 Tottenham

Current situation pa Half Time Arsenal 2 Vs 1 Tottenham
15/01/2025

Current situation pa Half Time

Arsenal 2 Vs 1 Tottenham

Address

Kanjedza Zeka Road
Blantyre
BOX84

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when The Chord TV posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to The Chord TV:

Videos

Share

Category