Situation Malawi

Situation Malawi Situation Malawi brings you exclusive and news that is accurate.
(2)

Ka chilungamo aka.
05/01/2025

Ka chilungamo aka.

Mr. and Mrs. Wesley Mlozi  have died in a road accident in Ntcheu. Reports indicate that they were en route to a funeral...
05/01/2025

Mr. and Mrs. Wesley Mlozi have died in a road accident in Ntcheu. Reports indicate that they were en route to a funeral when the vehicle they were in collided with a heavy cement truck. May their souls rest in peace 🙏.

With Chuck Norris – I just got recognised as one of their top best! 🎉
05/01/2025

With Chuck Norris – I just got recognised as one of their top best! 🎉

  Mayi Mary Laini Kaude azaka 87 ochokera m'mudzi wa Matewere mdera la mfumu yayikulu Juma m'boma la Mulanje ali mu ulul...
05/01/2025



Mayi Mary Laini Kaude azaka 87 ochokera m'mudzi wa Matewere mdera la mfumu yayikulu Juma m'boma la Mulanje ali mu ululu pomwe anthu okwiya anawamenya usiku wa lachinayi sabata ino ati powaganizira kuti akumanga mvula.

A Catherine Namanya omwe ndi mdzukulu wa mayiwa ati anthuwa analowa m'nyumba ya mayiwa kudzera pa zenera ndikuyamba kuwagenda.

Iwo ati anthu ena oyandikira atamva phokoso la anthuwa anathamangira kunyumbayo komwe anawapulumutsa ndikuwatengela ku chipatala chaching'ono cha Namphungo ndipo anawatumiza kuchipatala chachikulu cha bomali komwe anawagoneka kwa masiku awiri akulandira thandizo.

Pakadali pano m'neneri wa apolisi m'bomali Innocent Moses wati timupase nthawi asanaikepo ndemanga pa nkhaniyi.

Polakhula ndi mkulu wa bungwe lomenyera ufulu wa anthu achikulire m'dziko muno la MANEPO a Andrew Kavala apempha apolisi kufufuza zankhaniyi ndikuonesetsa kuti malamulo agwira ntchito kwa anthu omwe anachita zaupanduzi.

President Biden awarded the Presidential Medal of Freedom to 19 great leaders who have made America a better place. That...
05/01/2025

President Biden awarded the Presidential Medal of Freedom to 19 great leaders who have made America a better place. That included Denzel Washington 🎥.

05/01/2025

Ngati chibwenzi chako chakupempha kuti uchitumizire malichocho ako iweyo ndi kutumizadi nonse mitu yanu ndi yofoira. Zikuchita kuonekeratu kuti khalidwe lanu ndi la chisembwere and it shows that you have been sharing your beans 🫘 to many 😀. Ifeyo zikatipeza nyembazo tizikuyalutsani chifukwa we want to reduce this behavior. We don't want our kids to adopt that 😢 coz we ain't raising prostitutes we are raising good citizens for our country.

Kodi ndikuoneka kuti ndikulira kapena ndikuyankhura chilungamo?
05/01/2025

Kodi ndikuoneka kuti ndikulira kapena ndikuyankhura chilungamo?

Mbuzi ina ya MP yomwe ikupopedwa ndi Chakwera ndi iyi.... wakara akuimira uphungu koma amangolephera chifukwa cha zipani...
05/01/2025

Mbuzi ina ya MP yomwe ikupopedwa ndi Chakwera ndi iyi.... wakara akuimira uphungu koma amangolephera chifukwa cha zipani zomwe amaimira kenako analowa DPP pompo pompo anthu aku Zomba Chisi anamuvotera. Lero dzimbiri lose latha wayamba kunyoza DPP-APM uyu chaka chino ku Zomba asaimirenso Dpp akaimire Kongersi tione ngati anthu atazamuvotere.

Chaka kungoyamba ndi ma scandal eish.
05/01/2025

Chaka kungoyamba ndi ma scandal eish.

Fuel crisis in Malawi under President Chakwera.
04/01/2025

Fuel crisis in Malawi under President Chakwera.

04/01/2025

Dr. Kaliati wayamikira ulamuliro wa Dr. Bakili Muluzi, Prof Bingu wa Mutharika ndi Prof Peter Mutharika- APM. Kuti munthawi yawo ndalama imafikira aliyense.

04/01/2025

Kaliati akuti anthu aku Lilongwe akuchita ulimi wa mikodzo. Nkhwani othiliridwa ndi mikodzo koma ukoko ku Lilongwe mukudyesedwa mabi sure 🤣🤣. Boma ili tiona vinthu.

Vasilini wa komba mpaka K7 sauzande ndi mwana wache eish.
04/01/2025

Vasilini wa komba mpaka K7 sauzande ndi mwana wache eish.

Koma Alexious Kamangila ali moyo? Wangoti ziii ndimomwe ma Pitbull  🐕 alusira kunjaku we have to check on each other mor...
04/01/2025

Koma Alexious Kamangila ali moyo? Wangoti ziii ndimomwe ma Pitbull 🐕 alusira kunjaku we have to check on each other more especially ma Activist.

04/01/2025

anu ndi Chakwera wanuyo!!

Any idea comes from evils should not be recommended.

Ophunzira mu sukulu zaukachenjede zaboma ayamikira mtsogoleri wadziko lino Lazarus Chakwera kamba kokhazikitsa unduna wapadera oyang'anira maphunziro aku sukulu -zi.

Poyankhula ndi MIJ Online, Gershom Nyirenda mtsogoleri wabungwe la ophunzirawa lotchedwa Malawi Public Universities Students Union -MAPUSU wati kukhazikitsidwa kwa undunawu kuthandizira kuthana ndi mavuto omwe ophunzira amakumana nawo.

Iye wati zomwe zachitikazi zikuonetsa chidwi chomwe boma lili nacho popititsa patsogolo umoyo wa ophunzira mu sukulu zaukachenjede mdziko muno.

Unduna watsopanowu uzitsogozedwa ndi Dr Jessie Kabwira.

APM is everywhere.
04/01/2025

APM is everywhere.

UTM komanso Chilima Family have to sue Chakwera and Malawi Congress Party for kiling innocent Chilima. Ndipo mlandu ukuy...
04/01/2025

UTM komanso Chilima Family have to sue Chakwera and Malawi Congress Party for kiling innocent Chilima. Ndipo mlandu ukuyenera kuyamba pano atifotokozere chifukwa Chomveka chomwe anamuphera Chilima kulephera apo Chakwera ndi Kongersi yake sakuyenera kuzapikisana nawo pa zisankho zikibwerazi chifukwa ndi anthu akupha. We don't want criminals to lead us again! UTM SKC Legacy

  🤣🤣🤣🤣🤣Omwe azithandizira achitetezo pogwira akaidi omwe athawa ku ndende, tsopano azilandira thumba la chimanga la ma k...
04/01/2025

🤣🤣🤣🤣🤣

Omwe azithandizira achitetezo pogwira akaidi omwe athawa ku ndende, tsopano azilandira thumba la chimanga la ma kilo 50 ngati njira imodzi yowathokoza.

Mkulu woyang'anira ndende mchigawo chapakati a Bazirio Chapuwala ndiomwe alamula ndende zonse za mchigawo cha pakati ziyambe kutsatira izi.

Polankhura pa chikondwelero cha chaka chatsopano chomwe akuluakulu a ndende adali nacho mu mzinda wa Lilongwe, a Chapuwala ati izi zithandiza kuti anthu a mmadera (civilians) adzitha kuthandizapo pogwira akaidi omwe amathawa.

"Nthawi zambiri anthu samaona chowalimbikitsa kuti athandize achitetezo kugwira akaidi omwe athawa kundende koma pano omwe agwira mkaidi othawa adzilandira thumba la chimanga ndipo ngati wagwira akaidi awiri ndiye kuti matumba awiri amenewo. Ngati waona akaidi 5, dziwa kuti ndi matumba 5 a chimanga 5 amenewo," atero a Chapuwala.

Iwo ati izi zithandiza chifukwa anthu a mmadera adzigwira mkaidi yemwe wathawa kapena kukamuneneza ku polisi, chifukwa pali chowalimbikitsa kutero.

Chimangachi ati chizichokera minda yomwe ndendezi ili nayo.

Nthambi ya ndendede yati mchaka chathachi yakumana ndi vuto la kuthawa kwa akaidi

Address

Blantyre
BOX1997BLANTYRE

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Situation Malawi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Videos

Share