ToniCity 265

ToniCity 265 Your Favourite Beat Plug
(2)

Another day another dollar.. Let's make good music..
30/01/2025

Another day another dollar.. Let's make good music..

29/01/2025
29/01/2025

Pena ukazanvera nyimbo zake umazabalalika kuona ngati ndi mlongo amene akuimbayo chifukwa Cha mau anthetemya. Tremone Trun ndidolo kwambili ndipo landila maluwa Ako nzanga.

He's dropping a new song pompano koma zisanatelo tatiyeni tikaipase moto pa TikTok
[Link in the comment section]

28/01/2025

LOADED

🔥🔥New free beat alert🔥🔥
28/01/2025

🔥🔥New free beat alert🔥🔥

💸💰DOWNLOAD/BUY: beatstars.com/tonicityTERMS• This beat is only free for profit on non-streaming platforms (YouTube, SoundCloud, etc.) and appropriate credi...

26/01/2025

Some of the songs I have produced before PART ONE!!

20/01/2025

Good morning.

Chaka cha nyowani nde ndichimenechi ofunika kuyambapo fast!

Ndilankhuleni time ya bho tikunge nyimbo zotchyakuka bwino!

20/12/2024

Pamene 'Mubwere December' challenge ikukolela ku tiktok, mwini nyimbo Tremone Trun watulukila nkunena kuti pa 27 December pa asankha video imodzi imene yabhebha kwambiri ndipo apeleka K100,000 kwa amene wayichemetsayo.

Tremone wati iyi ndi challenge yokodola otchona amene amati abwela December kuwakumbutsa kuti December uja tsopano wakwana. Zonse zikuchitika apa https://vm.tiktok.com/ZMk6U2VWp/

Tiyeni nayoni challenge mudyepo kenakake
18/12/2024

Tiyeni nayoni challenge mudyepo kenakake

Ku Tiktok ndiuku kwabeba kale🔥, PA 27 ndisankha video imodzi yomwe iwine MK100, 000. kwaomwe amatha Kutchola BATCHA! . MUBWELE DECEMBER UJA AKUFUNIKA DANSI!. Show how good you are by clicking on the link provided below, Tivine mpaka matchona abwelele Kunyumba inu!! 😂🔥🔥. More info is provided on artwork. You can join with the Tiktok link below: https://vm.tiktok.com/ZMkjUeCQa/

18/12/2024

Tremone Trun - Mubwere December

17/12/2024

Eh eh pepani guys lol
12/12/2024

Eh eh pepani guys lol

" Usatinyase, Usatibhowe, ndipo Usatikande pokhalila. Kodi tinatchula chaka ngati ? "

AMalawi amene adatchona kunja awukila mwana uyu Tremone Trun , amene wayimba nyimbo yowakodola kuti amangoti abwela December koma osabwela.

12/12/2024

Officially out 🔥🔥

New music now out! 🔥 Tremone Trun - Mubwere December Produced by MeMixed and mastered by  Tcheyaman Mod Beats Video by G...
12/12/2024

New music now out! 🔥

Tremone Trun - Mubwere December

Produced by Me
Mixed and mastered by Tcheyaman Mod Beats
Video by
Guitars by
Recorded by Kalax Mw
Audio artwork by

Video Production by Audio Production by ã‚šviral

Tili momo
05/12/2024

Tili momo

Address

Blantyre

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when ToniCity 265 posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to ToniCity 265:

Videos

Share

Category