APHUNGU KU NYUMBA YA MALAMULO AGAWIKANA
Wolemba: Robert Edward
Aphungu anyumba yamalamulo asiyanaso maganizo kachitatu kumasana kuno.
Aphunguwa akugawikana maganizo pa fundo yoti a Sameer Suleiman a chipani cha DPP awachotse pa udindo wa wapampando wa komitti ya za ulimi mnyumbayi ati chifukwa choti akumabweretsa chisokonezo mnyumbayi.
Pakadali aphunguwa akuyenela Kuvota Ngati akuyenela kuweluka kapena kupitilila ndi zokambilana.
Koma asanayamba kuvotaku nduna ya zamalonda , Sosten Gwengwe adandaula kuti munthu wina wawagenda ndi botolo la madzi .
LIMBE POLICE ARREST WOMAN FOR VANDALIZING BWB PIPE
By Noel Mkwaila, BLANTYRE
Police in Limbe, Blantyre have arrested a 21 year old woman, Cecilia Ganya fir allegedly vandalizing Blantyre Water Board-BWB pipe in Bangwe Township in Blantyre.
Limbe Police spokesperson, Aubrey Singanyama says the suspect broke a temporary fixed broken pipe to access free water from BWB.
A viral social media video clip we have seen is showing the woman disconnecting the pipe and drawing water.
Singanyama says Ganya will appear in court soon to answer charges related to vandalism.
She hails from Ganya Village in the area of Traditional Authority Ganya in Ntcheu district.
#TheRadar #TruthUncensored
Earlier on Friday, President Lazarus Chakwera's convoy clashed with a funeral procession from Ndirande Township in Blantyre.
Watch the video below from the social media;
#TheRadar #TruthUncensored
Anthu ena m'boma la Mangochi anaimba nyimbo zotamanda omenyera ufulu Bon Kalindo yemwe amutulutsa pa belo lero, Lachisanu.
Kalindo akumuzenga mulandu osonkhezera zipolowe zomwe zidachitika m'bomali zokwiya ndi kugwa kwa ndalama ya kwacha.
Polankhula ndi anthuwa, Kalindo wati anthu asamaope kulankhula za kukhosi mdziko muno popeza ali ndi ufulu otero.
Pa zionetserozi, katundu ochuluka kuphatikizapo galimoto khumi akuti zinasakazidwa.
Mulanduwu awuimitsa kufikira pa 11 January chaka cha mawa.
#TheRadar #TruthUncensored
#nankhumwapressbriefing
One of the DPP presidential aspirants Kondwani Nankhumwa has now arrived at the Golden Peacock Hotel in Blantyre to address the media where he is expected to officially declare his interest to contest.
Hundreds of people have welcomed him with songs in his praise.
By Noel Mkwaila, BLANTYRE
#TheRadar #TruthUncensored
#airteltop8cup
NOMADS IN NO SHOW STILL
Noel Mkwaila, BLANTYRE
Silver Strikers are warming up for the second league game against Mighty Mukuru Wanderers in the Airtel Top 8 Cup at the Kamuzu Stadium in Blantyre.
But the hosts are not yet here with just a few minutes to the kick off.
Wanderers officials are still protesting the FAM ruling against them following the abandoned game and fracas in the first leg at the Bingu National Stadium.
#TheRadar #TruthUncensored
Anthu ena omwe amachita zionetsero ku Mangochi kummawaku zokakamiza boma kukonza zinthu maka pa chuma mdziko muno akuti aphwanya galimoto zina ku ofesi ya DC m'bomali.
Izi zinapangitsa apolisi kuyamba kuphulitsa utsi okhetsa misonzi kubalalitsa omwe anayamba za zipolowewa.
Mkulu wa gulu la Malawi First, Bon Kalindo yemwe amatsogolera zionetserozi sadalankhule nafe kuti timve chomwe chinachititsa kuti anthu ayambe kugenda.
Koma malipoti akuti apolisi anjata anthu angapo molingana ndi nkhaniyi. Nawonso apolisi sadalankhule.
#TheRadar #TruthUncensored
Kanema: Masamba a mchezo
#ParliamentAntiCorruptionParade
LAWMAKERS ENGAGE IN ANTI-CORRUPTION PARADE
By Robert Edward, LILONGWE
Malawian lawmakers are this morning engaged in an anti-corruption parade currently underway in Lilongwe having started from the Indipendence Drive Total Energies filling station to the Parliament Building.
This is part of commemorations marking 25 years since the establishment of the Anti-Corruption Bureau in the country.
At a recent public debate, the bureau's chief Chizuma decried inconsistent political will in the fight against corruption during these years.
She said: "There have been times when you could have political will, but that space is very narrow and very short such that if you don’t utilise it, it passes very quickly and gets closed.”
During the 25 years, ACB registered and processed 36 878 case. 26 210 of these were either closed or referred to other institutions while 10 615 were recommended for investigations.
#TheRadar #TruthUncensored
Some Karonga United supporters have reportedly denied FCB Nyasa Big Bullets to train at Karonga Stadium ahead of the teams' TNM Super League encounter tommorow.
Reasons for the supporters' actions remain unknown.
Super League of Malawi and Bullets officials are yet to comment on the matter.
#TheRadar #TruthUncensored
Video credit: Social media
#malawifirstprotests_update
The demonstrations have gained momentum at Nandozi in Blantyre where a lot of people have joined.
Bon Kalindo is addressing the protesters on a number of issues including a line up of their planned demos ahead
By Noel Mkwaila, BLANTYRE
#TheRadar #TruthUncensored
#MalawiFirstProtests_Update
Kalindo addresses a handful protesters around Malawi University of Business and Applied Sciences-MUBAS on their way to deliver a petition to Blantyre District Commissioner's office pushing for the resignation of President Chakwera over the prevailing economic hardships.
Video and text by Noel Mwala, BLANTYRE
#TheRadar #TruthUncensored