Chitemwe Media

Chitemwe Media Film/Video Production plus News.

26/01/2025
Ma handover, Trump to rule USA again
20/01/2025

Ma handover, Trump to rule USA again

19/01/2025



Mvula ikhoza kugona padenga
💦🌧️☔

17/01/2025


"Malawi Electoral Commission MEC ichitanso kalembela wachibwereza kuyambira pa 21 January mpaka pa 3 February." Watero komishona Mtalimanja

Ma studio opanga ma filimu akhuzika nawo pa moto omwe ukuyaka ku Los Angeles, California. Panopa chiwerengelo cha omwe a...
13/01/2025

Ma studio opanga ma filimu akhuzika nawo pa moto omwe ukuyaka ku Los Angeles, California. Panopa chiwerengelo cha omwe afa ndi 24 ndipo 16 asowa.

Malingana ndi ma report a CNN pali chiopsezo choti mphepo yomwe ikukwelezela motowu ipitilira ndipo likhoza kufika lachitatu moto ukuyakabe.

Suleiman ali mkati tikunena pano. Malingana ndi chikalata chomumangilacho ati kamba kakuyankhulitsa pa social media
06/01/2025

Suleiman ali mkati tikunena pano. Malingana ndi chikalata chomumangilacho ati kamba kakuyankhulitsa pa social media

05/01/2025

Umu ndi mmene zayendela ku zisankho za bungwe loona za ma kanema la Film Association of Malawi (FAMA:
Winners

■PRESIDENT - 81 Votes

1- Dorothy Kingston - 66
2- Flora Suya - 15

■VICE PRESIDENT 78 Votes
1- Kelvin Ngoma - 0
2- Gilbert Moyo - 31
3- Dickson Mandota - 29
4- Philimon Kuipa - 17

■ SECRETARY
1- Mr Ignatious Kaphinde

■ VICE SECRETARY
1- Charles Levison

■ TREASURER GENERAL
1- Mr Daud Shaib

■ VICE TREASURER
1- Catherine Kawawa

■ COMMITEE MEMBER
1- Daniel Quinn
2- Neria Chikhosi
3- Chiyembekezo Kalonga
4- Disiree Namachotsa

Kuli masankho ku bungwe la Film Association of Malawi. Chinkulilano chakula pakati pa azimayi awiri omwe akupikisana pa ...
05/01/2025

Kuli masankho ku bungwe la Film Association of Malawi. Chinkulilano chakula pakati pa azimayi awiri omwe akupikisana pa mpando wa utsogoleri wa bungweli. Flora Suya oziwika bwino pa nkhani ya ma kanema komanso Dorothy Kingston yemwe amaziwika mmatsamba anchezo ndi kutukula maluso komanso malonda. Masankhowa achitika lero ku Golden Peacock mumzinda wa Lilongwe

 Chakwera has moved Zikhale ng'oma and replaced him with Ezekiel ngoma with Jessy kabwila taking mistry of education.he ...
01/01/2025


Chakwera has moved Zikhale ng'oma and replaced him with Ezekiel ngoma with Jessy kabwila taking mistry of education.

he has also created new ministrial post of minister of state and service delivery and kambauwo wilima being minister of secondary and basic education. Ng'oma has been moved to Ministry of Mining.

Anthu ali nzipongwe kobasi kkkk
30/12/2024

Anthu ali nzipongwe kobasi kkkk

A science atayijambula nyerere ndi makina a macroscope ati umu ndi mmene nyerere imaonekela nkhope yake
26/12/2024

A science atayijambula nyerere ndi makina a macroscope ati umu ndi mmene nyerere imaonekela nkhope yake

For storage:
22/12/2024

For storage:

Anganga Ajabiru has been voted as 2024 Best Comedian by Muslim Arts Awards.
20/12/2024

Anganga Ajabiru has been voted as 2024 Best Comedian by Muslim Arts Awards.

Zonse zokonzekela mwambo wa Muslim Awards zatheka ndipo mwambowu uyamba nthawi iliyonse madzulo ano ku Amaryllis Hotel m...
20/12/2024

Zonse zokonzekela mwambo wa Muslim Awards zatheka ndipo mwambowu uyamba nthawi iliyonse madzulo ano ku Amaryllis Hotel mu mzinda wa Blantyre ndipo anthu ayamba kale kusonkhana.

Pa mwambowu a Muslim Awards akufuna apeleke mphoto kwa anthu asilamu a luso monga zisuzo, ndakatulo komanso ogwira ntchito zolemba nkuulutsa nkhani kungotchulapo ochepa.

Pambuyo pophunzitsidwa Luso losiyanasiyana ku kuchokela ku Luso Technical College, iyi inali nthawi yolandila ma certifi...
07/12/2024

Pambuyo pophunzitsidwa Luso losiyanasiyana ku kuchokela ku Luso Technical College, iyi inali nthawi yolandila ma certificate lachisanu ku Blantyre Lodge mu mzinda wa Blantyre. Ophunzira opyola makumi asanu ndi omwe atsiriza nkulandira zida zoyambira.

Mwambo ngati omwewu unachitika masabata awiri apitawo mu mzinda wa Lilongwe kumenenso ophunzira a mchigawo cha pakati analandila ma certificate.

Address

Along Chipembere Highway
Blantyre
P.OBOX;90307,BANGWE

Telephone

+265998192747

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Chitemwe Media posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Chitemwe Media:

Videos

Share