Poniciah uja ndine

Poniciah uja ndine famous Ni**er I lke way i'm

18/04/2023

Alinse azipanga zake

08/04/2023

Collabo opandadi k banton ndekuti singabhebhe ndizoona guys eeee K Banton ndi dolo

09/03/2023

Ubwino wake tonse ndife chifanizo Cha ambuye or mutisale chimo ndilanu

20/02/2023

Akuti timakondana ngati shubu ndi theyela zachambazi bas

14/01/2023

Ngati sumafila zomwe ndimapanga ingotseka maso

01/01/2023

Happy New year to all my team bhebhetsa

09/12/2022

Mwayi wanga ndi soka lawina
Wina uku zamuonekera ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚ nyimbo eli njuchi zitaya

26/11/2022

School report ija zokhe waphweteka nice song ๐Ÿ’ฏโ˜‘๏ธ

19/11/2022

Zikomo ambuye pazomwe mwachita pondifikisa tsiku lalero
Mutamandike Baba ๐Ÿ™๐Ÿ™

18/11/2022

Friday ndi wozzah, Saturday ndi wozzah
Vibe song by K BANTON Wozzah ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ”ฅ

17/11/2022

Anagova zoti zanga ubweza pano akufuna chibweleza ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚ song dzanga ubweza by Guntolah

17/11/2022

Chiyambi chamantha ndikuvula Malaya pandewu ๐Ÿต๐Ÿต๐Ÿต๐Ÿต

17/11/2022

Akadzi ena timapasirana ngati tikudya fodya wayembasi pakena nyasa fodya, ukamuona dzako nawe umati ndidye nawo ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚ nyimbo mpunga wanyama by guntolah

17/11/2022

Zachamba moti tizilota ndalama kumalotanazo ma ex pali nzeru apa please ambuye muyendela chiwanda cholota ma ex chitheletu ๐Ÿ™๐Ÿ™๐Ÿ™

17/11/2022

Thanks God for give me another chapter Amen

16/11/2022

Nyimbo mpunga wanyama louder koma guntolah iweyo ๐ŸŒŸ

16/11/2022

Akadzi enawa tidzigodya nawo not dating guys, ndipatseni mpunga wanyama ndi ka drink basi

14/11/2022

Kwacha timve mavuto akumalawi

13/11/2022

Zikuti bwaji kwanuko zankhani zachimanga kuno 32,000.00 kwacha 50 kg

13/11/2022

Ndibwino kupeza kadzi wamutu wang'ono kupewa kutha ndalama zambiri ndimutu wawukulu ku saloon ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚ boys take note

13/11/2022

Kukhala kumalawi ndikupilira

13/11/2022

Kadzi alingati katoti komwe madolo amamwelamo mowa , zoti gulu lotse amagwiritsa ntchito nde akadziwa nditimatoti tamowa toti wina aliyense amadyako๐Ÿ˜†๐Ÿ˜†๐Ÿ˜†

13/11/2022

KOMA GUNTOLAH IWEYO
Mawulemu inu simunthu wamba
Mpunga wanyama yomweyo
๐Ÿ™Œ๐Ÿ™Œ๐Ÿ™Œ๐Ÿ™Œ

12/11/2022

Chalaka baka khuku singatole ndekuti Peter uja ngati zinamuvuta Lazarus chakwera sangakwanitse dzikoli kulamulira

12/11/2022

Kadzi opita kuchezo muzagoziwa kuti ndi hulu ameneo pothelatu

12/11/2022

Boys mwatani Kodi pakana bayara mwadyelatso kadza wake
Zilikuno guys wina wabesa dollar ndi kadzi kkkkkkk ๐Ÿ˜†๐Ÿ˜†๐Ÿ˜†๐Ÿ˜†

12/11/2022

Muli busy kuba ndalama zaboma kumati ndinu ochita bwino Kona chosecho ndinu osauka kupanda misokho yathu muli ndani inu, kuti mudye ndimisokho yathu

12/11/2022

Gahena tikumuonela Malawi momuno ayi koma zafikapo ๐Ÿ™Œ๐Ÿ™Œ

11/11/2022

Half best is like half of contract yogodyana kkkkkkkk wina kumati alichikondi ๐Ÿ’”๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚

11/11/2022

Akuti mtima sumavala tsadza koma mene zafikilamu Ku MALAWI Kuno eeeee matsadzaza aja tivalabe
Kubadwira kumalawi ndikulimba mtima

Address

London
TESHA

Telephone

+265993211987

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Poniciah uja ndine posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category



You may also like